Zephaniah 1:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu okhala ku chigwa cha mzinda lirani komvetsa chisoni, chifukwa amalonda onse atha, onse ogulitsa siliva aonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chemani okhala m'chigwa, pakuti amalonda onse atayika, onsewo osenza siliva aonongeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lirani mwachisoni, inu amene mumakhala kumene kuli msika; a malonda anu onse adzapululidwa, ndiponso onse amene ali ndi siliva adzawonongedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cemani okhala m'cigwa, pakuti amalonda onse atayika, onsewo osenza siliva aonongeka.