Zephaniah 1:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku limenelo kudzamveka lipenga ndi kufuula kwankhondo, kwa asilikali othira nkhondo mizinda ya malinga ndiponso nsanja zankhondo za Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
tsiku la lipenga ndi lakufuulira midzi yamlinga, ndi nsanja zazitali za kungodya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku loliza lipenga ndi la mfuwu wankhondo, tsiku la kugwa kwa mizinda yotetezedwa ndi nsanja za pa ngodya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
tsiku la lipenga ndi lakupfuulira midzi yamalinga, ndi nsanja zazitali za kungondya.