Zephaniah 1:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Pa tsiku limenelo la nsembe yanga ndidzalanga ana a mfumu ndi akalonga ake, ndi onse otengera zachilendo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzachitika tsiku la nsembe ya Yehova, kuti ndidzalanga akalonga ndi ana a mfumu, ndi onse akuvala chovala chachilendo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku la nsembe ya Yehova ndidzalanga akalonga ndi ana aamuna a mfumu ndi onse amene amavala zovala zachilendo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzacitika tsiku la nsembe ya Yehova, kuti ndidzalanga akalonga ndi ana a mfumu, ndi onse akubvala cobvala cacilendo.