Zephaniah 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimenechi chidzakhala chilango choyenerera kunyada kwaoko, chifukwa adanyoza anthu a Chauta Wamphamvuzonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi adzakhala nacho m'malo mwa kudzikuza kwao, chifukwa anatonza, nadzikuza pa anthu a Yehova wa makamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ichi ndi chimene adzalandire chifukwa cha kunyada kwawo, chifukwa chonyoza ndi kuchitira chipongwe anthu a Yehova Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici adzakhala naco m'malo mwa kudzikuza kwao, cifukwa anatonza, nadzikuza pa anthu a Yehova wa makamu.