Zephaniah 2:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzasamulira dzanja lake kumpoto ndi kuwononga dziko la Asiriya. Mzinda wa Ninive adzausandutsa bwinja, udzakhala wagwaa ngati chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzatambasulira dzanja lake kumpoto nadzaononga Asiriya, nadzasanduliza Ninive akhale bwinja, wouma ngati chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndi kuwononga Asiriya, kusiya Ninive atawonongekeratu ndi owuma ngati chipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzatambasulira dzanja lace kumpoto nadzaononga Asuri, nadzasanduliza Nineve akhale bwinja, wouma ngati cipululu.