Zephaniah 2:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzinda wa Gaza udzasiyidwa, Asikeloni adzasanduka bwinja. Anthu a ku Asidodi adzapirikitsidwa masana mwadzidzidzi, Akeroni adzapasuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Gaza adzasiyidwa, ndi Asikeloni adzakhala bwinja; adzaingitsa Asidodi usana, ndi Ekeroni adzazulidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gaza adzasiyidwa ndipo Asikeloni adzasanduka bwinja. Nthawi yamasana Asidodi adzakhala wopanda anthu ndipo Ekroni adzazulidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Gaza adzasiyidwa, ndi Asikeloni adzakhala bwinja; adzaingitsa Asidodi usana, ndi Ekroni adzazulidwa.