Zephaniah 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko limene lili m'mphepete mwa nyanja, lidzasanduka madambo a abusa, ndi makola a nkhosa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo dziko la kunyanja lidzakhala busa, ndi mapanga a abusa, ndi makola a zoweta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko la mʼmbali mwa nyanja, kumene kumakhala Akereti, lidzakhala malo a abusa ndi la makola a nkhosa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo dziko la kunyanja lidzakhala husa, ndi mapanga a abusa, ndi makola a zoweta.