Zephaniah 2:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Ndamva kunyoza kwa Amowabu, ndiponso kutukwana kwa Aamoni, m'mene anyozera anthu anga ndi m'mene adzikuzira m'dziko mwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinamva kutonza kwa Mowabu ndi matukwano a ana a Amoni, zimene anatonza nazo anthu anga, ndi kudzikuza pa malire ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndamva kunyoza kwa Mowabu ndi chipongwe cha Amoni, amene ananyoza anthu anga ndi kuopseza kuti alanda dziko lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinamva kutonza kwa Moabu ndi matukwano a ana a Amoni, zimene anatonza nazo anthu anga, ndi kudzikuza pa malire ao.