Psalms 89
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
2Pakuti ndinati, Cifundo adzacimanga kosaleka; Mudzakhazika cikhulupiriko canu m'Mwamba mweni mweni.
4Ndidzakhazika mbeu yako ku nthawi yonse, Ndipo ndidzamanga mpando wacifumu wako ku mibadwo mibadwo.