bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
1 Chronicles 25
1 Chronicles 25
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 24
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 26 →
1
Ndipo Davide ndi akazembe a gulu la nkhondo anapatulira utumikiwo ena a ana a Asafu, ndi a Hemani, ndi a Yedutuni, anenere ndi azeze, ndi zisakasa, ndi nsanje; ndi ciwerengo ca anchito monga mwa kutumikira kwao ndko:
2
a ana a Asafu: Zakuri, ndi Yosefe, ndi Netaniya, ndi Asarela, ana a Asafu; mwa cilangizo ca Asafu, wakunenera mwa cilangizo ca mfumu.
3
A Yedntuni, ana a Yedutuni: Gedaliya, ndi Zeri, ndi Yesaya, Hasabiya, ndi Matitiya, asanu ndi mmodzi; mwa cilangizo ca atate wao Yedutuni, ndiye wakunenera ndi kuyamika ndi kulemekeza Yehova ndi zeze.
4
A Hemani, ana a Hemani: Bukiya, Mataniya, Uziyeli, Sebuyeli, ndi Yerimoti, Hananiya, Hanani, Eliyata, Gidaliti, ndi Romamti-Ezeri, Yosibekasa, Maloti, Hotiri, Mahazioti;
5
awa onse ndiwo ana a Hemani mlauli wa mfumu m'mau a Mulungu, kuti akweze mphamvu yace. Ndipo Mulungu anapatsa Hemani ana amuna khumi ndi anai, ndi ana akazi atatu.
6
Onsewa anawalangiza ndi atate wao ayimbe m'nyumba ya Yehova ndi nsanje, zisakasa ndi azeze; atumikire nazo m'nyumba ya Mulungu; ndipo Asafu, Yedutuni, ndi Hemani, anawalangiza ndi mfumu.
7
Ndipo ciwerengo cao, pamodzi ndi abale ao ophunzitsidwa ayimbire Yehova, onse anthetemya, ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu.
8
Ndipo anacita maere pa udikiro wao, analingana onse, ang'ono ndi akuru, mphunzitsi ndi wophunzira.
9
Maere oyamba tsono anagwera a banja la Asafu ndiye Yosefe; waciwiri Gedaliya, iye ndi abale ace, ndi ana ace khumi ndi awiri;
10
wacitatu Zakuri, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
11
wacinai Izri, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
12
wacisanu Netaniya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
13
wacisanu ndi cimodzi Bukiya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
14
wacisanu ndi ciwiri Yesarela: ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
15
wacisanu ndi citatu Yesaya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
16
wacisanu ndi cinai Mataniya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri:
17
wakhumi Simeyi, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
18
wakhumi ndi cimodzi Azareli, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
19
wakhumi ndi ciwiri Hasabiya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
20
wakhumi ndi citatu Subaeli, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
21
wakhumi ndi cinai Matitiya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
22
wakhumi ndi cisanu Yeremoti, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
23
wakhumi ndi cisanu ndi cimodzi Hananiya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
24
wakhumi ndi cisanu ndi ciwiri Yosibekasa, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
25
wakhumi ndi cisanu ndi citatu Hanani, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
26
wakhumi ndi cisanu ndi cinai Maloti, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
27
wa makumi awiri Eliyata, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
28
wa makumi awiri ndi cimodzi Hotiri, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
29
wa makumi awiri ndi ciwiri Gidaliti, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
30
wa makumi awiri ndi citatu Mahazioti, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;
31
wa makumi awiri ndi cinai RomamtiEzeri, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri.
← Chapter 24
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 26 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29