bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
/
Joshua 19
Joshua 19
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
← Chapter 18
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 20 →
1
Ndipo maere achiwiri anamtulukira Simeoni, fuko la ana a Simeoni monga mwa mabanja ao; ndi cholowa chao chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.
2
Ndipo anali nacho cholowa chao Beereseba, kapena Sheba, ndi Molada;
3
ndi Hazara-Suwala, ndi Bala, ndi Ezemu;
4
ndi Elitoladi, ndi Betuli, ndi Horoma;
5
ndi Zikilagi, ndi Betemara-Kaboti, ndi Hazara-Susa:
6
ndi Betelebaoti, ndi Saruheni; midzi khumi ndi itatu ndi milaga yao;
7
Aini, Rimoni ndi Eteri ndi Asani; midzi inai ndi milaga yao;
8
ndi milaga yonse yozungulira midzi iyi mpaka Baalati-Bere ndiwo Rama kumwera. Ndicho cholowa cha fuko la ana a Simeoni, monga mwa mabanja ao.
9
M'gawo la ana a Yuda muli cholowa cha ana a Simeoni; popeza gawo la ana a Yuda linawachulukira; chifukwa chake ana a Simeoni anali nacho cholowa pakati pa cholowa chao.
10
Ndipo maere achitatu anakwerera ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao; ndi malire a cholowa chao anafikira ku Saridi;
11
nakwera malire ao kunka kumadzulo ndi ku Mareyala nafikira ku Dabeseti, nafikira ku mtsinje wa patsogolo pa Yokoneamu;
12
ndi kuchokera ku Saridi anazungulira kunka kum'mawa kumatulukira dzuwa, mpaka malire a Kisiloti-Tabori; natuluka kunka ku Daberati, nakwera ku Yafiya;
13
ndi pochoka pamenepo anapitirira kunka kum'mawa ku Gatihefere, ku Etikazini; natuluka ku Rimoni umene ulembedwa mpaka ku Neya,
14
nauzungulira malire kumpoto, kunka ku Hanatoni; ndi matulukiro ake anali ku chigwa cha Ifutahele;
15
ndi Katati, ndi Nahalala ndi Simironi, ndi Idala ndi Betelehemu: midzi khumi ndi iwiri ndi milaga yao.
16
Ichi ndi cholowa cha ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao, midzi iyi ndi milaga yao.
17
Maere achinai anamtulukira Isakara, kunena za ana a Isakara monga mwa mabanja ao.
18
Ndi malire ao anali ku Yezireele, ndi Kesuloti, ndi Sunemu;
19
ndi Hafaraimu, ndi Siyoni, ndi Anaharati;
20
ndi Rabiti ndi Kisiyoni, ndi Ebezi;
21
ndi Remeti ndi Enganimu ndi Enihada, ndi Betepazezi;
22
ndi malire anafikira ku Tabori, ndi Sahazuma, ndi Betesemesi; ndi matulukiro a malire ao anali ku Yordani; midzi khumi ndi isanu ndi umodzi ndi milaga yao.
23
Ichi ndi cholowa cha fuko la ana a Isakara, monga mwa mabanja ao, midzi ndi milaga yao.
24
Ndipo maere achisanu analitulukira fuko la ana a Asere monga mwa mabanja ao.
25
Ndi malire ao ndiwo Helekati, ndi Hali, ndi Beteni ndi Akisafu;
26
ndi Alamumeleki, ndi Amada, ndi Misala; nafikira ku Karimele kumadzulo ndi ku Sihori-Libinati;
27
nazungulira kotulukira dzuwa ku Betedagoni, nafikira ku Zebuloni ndi ku chigwa cha Ifutahele, kumpoto ku Betemeke, ndi Neiyeli; natulukira ku Kabulu kulamanzere,
28
ndi Ebroni, ndi Rehobu, ndi Hamoni, ndi Kana, mpaka ku Sidoni wamkulu;
29
nazungulira malire kunka ku Rama, ndi kumudzi wa linga la Tiro; nazungulira malire kunka ku Hosa; ndi matulukiro ake anali kunyanja, kuchokera ku Mahalabu mpaka ku Akizibu;
30
Uma womwe ndi Afeki, ndi Rehobu; midzi makumi awiri mphambu iwiri ndi milaga yao.
31
Ichi ndi cholowa cha fuko la ana a Asere monga mwa mabanja ao, midzi iyi ndi milaga yao.
32
Maere achisanu ndi chimodzi anatulukira ana a Nafutali, ana a Nafutali monga mwa mabanja ao.
33
Ndipo malire ao anayambira ku Helefe ku thundu wa ku Zaananimu, ndi Adami-Nekebu, ndi Yabinele, mpaka ku Lakumu; ndi matulukiro ake anali ku Yordani;
34
nazungulira malire kunka kumadzulo ku Azinoti-Tabori, natulukira komweko kunka ku Hukoku; nafikira ku Zebuloni kumwera, nafikira ku Asere kumadzulo, ndi ku Yuda pa Yordani kum'mawa.
35
Ndipo midzi yamalinga ndiyo Zidimu, Zeri, ndi Hamati, Rakati, ndi Kinereti;
36
ndi Adama, ndi Rama, ndi Hazori;
37
ndi Kedesi, ndi Ederei, ndi Enihazori;
38
ndi Yironi, ndi Migidalele, Horemu, ndi Betanati, ndi Betesemesi; midzi khumi ndi isanu ndi inai, ndi milaga yao.
39
Ichi ndi cholowa cha fuko la ana a Nafutali, monga mwa mabanja ao, midzi ndi milaga yao.
40
Maere achisanu ndi chiwiri anatulukira fuko la ana a Dani, monga mwa mabanja ao.
41
Ndipo malire a cholowa chao anali Zora, ndi Esitaoli, ndi Irisemesi;
42
Saalabini, ndi Ayaloni ndi Itila;
43
ndi Eloni ndi Timna ndi Ekeroni;
44
ndi Eliteke, ndi Gibetoni, ndi Baalati;
45
ndi Yehudi, ndi Beneberaki, ndi Gatirimoni;
46
ndi Meyarikoni, ndi Rakoni, ndi malire pandunji pa Yopa.
47
Koma malire a ana a Dani anatuluka kupitirira iwowa; pakuti ana a Dani anakwera nathira nkhondo ku Lesemu, naulanda naukantha ndi lupanga lakuthwa, naulandira, nakhala m'mwemo, nautcha Lesemu, Dani; ndilo dzina la Dani atate wao.
48
Ichi ndi cholowa cha fuko la ana a Dani, monga mwa mabanja ao, midzi iyi ndi milaga yao.
49
Ndipo atatha kuligawa dziko likhale cholowa chao monga mwa malire ake, ana a Israele anapatsa Yoswa mwana wa Nuni cholowa pakati pao;
50
monga mwa lamulo la Yehova anampatsa mudzi umene anawapempha, ndiwo Timnati-Sera, ku mapiri a Efuremu; ndipo anamanga mudziwo nakhala m'mwemo.
51
Izi ndizo zolowa anazigawa Eleazara wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a nyumba za atate a mafuko a ana a Israele, zikhale zaozao, ndi kulota maere ku Silo pamaso pa Yehova ku khomo la chihema chokomanako. Momwemo anatha kuligawa dziko.
← Chapter 18
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 20 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24