bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
/
1 Chronicles 25
1 Chronicles 25
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
← Chapter 24
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 26 →
1
Ndipo Davide ndi akazembe a gulu la nkhondo anapatulira utumikiwo ena a ana a Asafu, ndi a Hemani, ndi a Yedutuni, anenere ndi azeze, ndi zisakasa, ndi nsanje; ndi chiwerengo cha antchito monga mwa kutumikira kwao ndicho:
2
a ana a Asafu: Zakuri, ndi Yosefe, ndi Netaniya, ndi Asarela, ana a Asafu; mwa chilangizo cha Asafu, wakunenera mwa chilangizo cha mfumu.
3
A Yedutuni, ana a Yedutuni: Gedaliya, ndi Zeri, ndi Yesaya, Hasabiya, ndi Matitiya, asanu ndi mmodzi; mwa chilangizo cha atate wao Yedutuni, ndiye wakunenera ndi kuyamika ndi kulemeza Yehova ndi zeze.
4
A Hemani, ana a Hemani: Bukiya, Mataniya, Uziyele, Sebuele, ndi Yerimoti, Hananiya, Hanani, Eliyata, Gidaliti, ndi Romamiti-Ezere, Yosibekasa, Maloti, Hotiri, Mahaziyoti;
5
awa onse ndiwo ana a Hemani mlauli wa mfumu m'mau a Mulungu, kuti akweze mphamvu yake. Ndipo Mulungu anapatsa Hemani ana amuna khumi ndi anai, ndi ana akazi atatu.
6
Onsewa anawalangiza ndi atate wao aimbe m'nyumba ya Yehova ndi nsanje, zisakasa ndi azeze; atumikire nazo m'nyumba ya Mulungu; ndipo Asafu, Yedutuni, ndi Hemani, anawalangiza ndi mfumu.
7
Ndipo chiwerengo chao, pamodzi ndi abale ao ophunzitsidwa aimbire Yehova, onse anthetemya, ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu.
8
Ndipo anachita maere pa udikiro wao, analingana onse, ang'ono ndi akulu, mphunzitsi ndi wophunzira.
9
Maere oyamba tsono anagwera a banja la Asafu ndiye Yosefe; wachiwiri Gedaliya, iye ndi abale ake, ndi ana ake khumi ndi awiri;
10
wachitatu Zakuri, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
11
wachinai Iziri, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
12
wachisanu Netaniya, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
13
wachisanu ndi chimodzi Bukiya, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
14
wachisanu ndi chiwiri Yesarela, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
15
wachisanu ndi chitatu Yesaya, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
16
wachisanu ndi chinai Mataniya, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
17
wakhumi Simei, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
18
wakhumi ndi chimodzi Azarele, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
19
wakhumi ndi chiwiri Hasabiya, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
20
wakhumi ndi chitatu Subaele, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
21
wakhumi ndi chinai Matitiya, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
22
wakhumi ndi chisanu Yeremoti, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
23
wakhumi ndi chisanu ndi chimodzi Hananiya, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
24
wakhumi ndi chisanu ndi chiwiri Yosibekasa, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
25
wakhumi ndi chisanu ndi chitatu Hanani, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
26
wakhumi ndi chisanu ndi chinai Maloti, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
27
wamakumi awiri Eliyata, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
28
wa makumi awiri ndi chimodzi Hotiri, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
29
wa makumi awiri ndi chiwiri Gidaliti, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
30
wa makumi awiri ndi chitatu Mahaziyoti, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri;
31
wa makumi awiri ndi chinai Romamiti-Ezere, ana ake ndi abale ake khumi ndi awiri.
← Chapter 24
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 26 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29