bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Hosea 3
Hosea 3
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 2
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 4 →
1
Tsono Chauta adandiwuza kuti, “Pitanso, ukakonde mkazi wachigololo amene ali ndi chibwenzi chake. Umkonde monga momwe Ine Chauta ndimakondera Israele, ngakhale iyeyo amapembedza milungu ina, ndipo amakonda kuitsirira nsembe za mphesa zabwino zoumika.”
2
Motero ndidamkwatira popereka ndalama khumi ndi zisanu zasiliva, ndiponso mitanga isanu ndi iŵiri ya barele.
3
Ndidamuuza mkaziyo kuti, “Uzikhala nane masiku ambiri, osachitanso zachiwerewere kapena chigololo ndi munthu wina. Nanenso ndidzachita chimodzimodzi.”
4
Ndiye kuti Aisraele adzakhala masiku ambiri opanda mafumu kapena akalonga, osapereka nsembe kapena kuimika miyala yachipembedzo, opanda zamaula kapena mafano oombezera.
5
Pambuyo pake Aisraelewo adzabwerera ndi kufunafuna Chauta Mulungu wao ndi mdzukulu wa Davide mfumu yao. Nthaŵi imeneyo Aisraele adzagonja kwa Chauta ndipo adzalandira zabwino zake.
← Chapter 2
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 4 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14