bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Leviticus 12
Leviticus 12
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 11
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 13 →
1
Chauta adauza Mose kuti,
2
“Uza Aisraele kuti mkazi akakhala ndi pakati, nabala mwana wamwamuna, adzakhala woipitsidwa masiku asanu ndi aŵiri, monga pa nthaŵi yake yakusamba.
3
Ndipo pa tsiku lachisanu ndi chitatu mwanayo aumbalidwe.
4
Mkaziyo adikirebe masiku ena 33, kuti ayeretsedwe ku matenda ake. Asakhudze kanthu kopatulika kalikonse, ndipo asaloŵe m'malo oyera, mpaka masiku akudziyeretsa atatha.
5
Koma akabala mwana wamkazi, adzakhala woipitsidwa masabata aŵiri monga pa nthaŵi yake yakusamba. Ndipo mkaziyo adikirebe masiku ena 66, kuti ayeretsedwe ku matenda ake.
6
“Tsono masiku akudziyeretsa kwake aja atatha, kapena ndi a mwana wamwamuna kapena a mwana wamkazi, abwere kwa wansembe ndi mwanawankhosa wa chaka chimodzi pa khomo la chihema chamsonkhano, kuti nkhosayo ikhale nsembe yopsereza. Abwerenso ndi bunda la nkhunda kapena njiŵa, kuti aperekere nsembe yopepesera machimo.
7
Wansembeyo apereke zimenezo pamaso pa Chauta potsata mwambo wopepesera mkaziyo. Apo mkaziyo adzakhala woyeretsedwa ku matenda ake. Limeneli ndi lamulo la mkazi amene abala mwana wamwamuna kapena wamkazi.
8
Koma ngati alibe mwanawankhosa, atenge njiŵa ziŵiri kapena maundaankhunda aŵiri, imodzi ikhale ya nsembe yopsereza, ndipo inayo ikhale ya nsembe yopepesera machimo. Tsono wansembe achite mwambo wopepesera, ndipo mkaziyo adzakhala woyeretsedwa.”
← Chapter 11
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 13 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27