bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 11
Job 11
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 10
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 12 →
1
Pamenepo anayankha Zofari wa ku Naama, nati,
2
Kodi mau ocurukawa sayenera kuwayankha? Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama?
3
Kodi zotamanda zako ziwatseke anthu pakamwa? Useka kodi, wopanda munthu wakukucititsapo manyazi?
4
Pakuti unena, Ciphunzitso canga ncoona, Ndipo ndiri woyera pamaso pako.
5
Koma, hal mwenzi atanena Mulungu, Ndi kukutsegulira milomo yace motsutsa;
6
Nakufotokozere zinsinsi za nzeru, Popeza zipindika-pindika macitidwe ao! Cifukwa cace dziwa kuti Mulungu akuiwalira mphulupulu zina.
7
Kodi ukhoza kupeza Mulungu mwa kufunafuna? Ukhoza kupeza Wamphamvuyonse motsindika?
8
Kumpeza kutalika ngati kumwamba, ungacitenji? Kuzama ngati kumanda, ungadziwenji?
9
Muyeso wace utalikira utali wace wa dziko lapansi, Citando cace ciposa ca nyanja.
10
Akapita, nakatsekera, Nakaturutsa bwalo la mlandu, adzamletsa ndani?
11
Pakuti adziwa anthu opanda pace, Napenyanso mphulupulu, ngakhale saisamalira.
12
Koma munthu wopanda pace asowa nzeru, Ngakhale munthu abadwa ngati mwana wa mbidzi.
13
Ukakonzeratu mtima wako, Ndi kumtambasulira Iye manja ako;
14
Mukakhala mphulupulu m'dzanja lako, uicotseretu kutali, Ndi cisalungamo cisakhale m'mahema mwako;
15
Popeza pamenepo udzakweza nkhope yako opanda banga; Nudzalimbika osacita mantha;
16
Pakuti udzaiwala cisoni cako, Udzacikumbukila ngati madzi opita;
17
Ndipo moyo wako udzayera koposa usana; Kungakhale kuli mdima kudzakhala ngati m'mawa.
18
Ndipo udzalimbika mtima popeza pali ciyembekezo; Nudzafunafuna, ndi kugona mosatekeseka,
19
Inde udzagona pansi, wopanda wina wakukunjenjemeretsa, Ndipo ambiri adzakupembedza,
20
Koma maso a oipa adzagoma, Ndi pothawirapo padzawasowa, Ndipo ciyembekezo cao ndico kupereka mzimu wao.
← Chapter 10
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 12 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42