bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 29
Job 29
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 28
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 30 →
1
Ndipo Yobu anaonjezanso mwambi wace, nati,
2
Ha! ndikadakhala monga m'miyezi yapitayi, Monga m'masiku akundisunga Mulungu;
3
Muja nyali yace inawala pamutu panga, Ndipo ndi kuunika kwace ndinayenda mumdima;
4
Monga umo ndinakhala m'masiku anga olimba, Muja uphungu wa Mulungu unakhala pahema panga;
5
Muja Wamphamvuyonse akali nane pamodzi, Ndi ana anga anandizinga;
6
Muja popondera ine padakhatamira ndi mafuta amkaka, Ndi thanthwe linanditsanulira mitsinje ya mafuta aazitona!
7
Muja ndinaturuka kumka kucipata kumudzi, Muja ndinakonza pokhala panga kukhwalala,
8
Anyamata anandiona nabisala, Okalamba anandinyamukira, nakhala ciriri,
9
Akalonga anadziletsa kulankhula, Ndi kugwira pakamwa pao;
10
Mau a omveka anali zi, Ndi lilime lao linamamatira ku malakalaka ao.
11
Pakuti pondimva ine khutu, linandidalitsa; Ndipo pondiona diso, linandicitira umboni.
12
Pakuti ndinapulumutsa wozunzika wakupfuula; Mwana wamasiye yemwe wosowa mthandizi.
13
Dalitso la iye akati atayike linandidzera, Ndi mtima wa mkazi wamasiye ndinauyimbitsa mokondwera.
14
Ndinabvala cilungamo, ndipo cinandibvala ine; Ciweruzo canga cinanga mwinjiro ndi nduwira.
15
Ndinali maso a akhungu, Ndi mapazi a otsimphina.
16
Ndinali atate wa waumphawi; Ndi mlandu wa iye amene sindinamdziwa ndinafunsitsa.
17
Ndipo ndinatyola nsagwada ya wosalungama, Ndi kukwatula cogwidwa kumano kwace.
18
Pamenepo ndinati, Ndidzatsirizika m'cisa canga; Ndipo ndidzacurukitsa masiku anga ngati mcenga.
19
Muzu wanga watambalala kufikira kumadzi; Ndi mame adzakhala pa nthambi yanga usiku wonse.
20
Ulemu wanga udzakhala wosaguga mwa ine, Ndi uta wanga udzakhala wosalifuka m'dzanja mwanga.
21
Anthu anandimvera, nalindira, Nakhala cete, kuti ndiwapangire.
22
Nditanena mau anga sanalankhulanso, Ndi kunena kwanga kunawakhera.
23
Anandilindira ngati kulindira mvula, Nayasama pakamwa pao ngati kulira mvula ya masika.
24
Ndinawaseka akapanda kulimbika mtima; Ndipo sanagwetsa kusangalala kwa nkhope yanga.
25
Ndinawasankhira njira yao ndi kukhala mkuru wao. Ndinakhala ngati mfumu mwa ankhondo ace, Ngati wotonthoza ofedwa.
← Chapter 28
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 30 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42