bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 16
Job 16
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 15
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 17 →
1
Pamenepo Yobu anayankha, nati,
2
Ndamva zambiri zotere; Inu nonse ndinu otonthoza mtima mondilemetsa.
3
Kodi adzatha mau ouluzika? Kapena cikuwindula nciani kuti uyankha zotere?
4
Inenso ndikadanena monga inu, Moyo wanu ukadakhala m'malo mwa moyo wanga, Ndikadalumikizanitsa mau akutsutsana nanu, Ndi kukupukusirani mutu wanga.
5
Koma ndikadakulimbikitsani ndi m'kamwa mwanga, Ndi citonthozo ca milomo yanga cikadatsitsa cisoni canu.
6
Cinkana ndinena cisoni canga sicitsika; Ndipo ndikaleka, cindicokera nciani?
7
Koma tsopano wandilemetsa Iye; Mwapasula msonkhano wanga wonse.
8
Kundigwira kwanu, ndiko umboni wonditsutsa, Kuonda kwanga kundiukira, kucita umboni pamaso panga.
9
Iye ananding'amba m'kundida kwace, nakwiya nane, Anandikukutira mano; Mdani wanga ananditong'olera maso ace.
10
Iwo anandiyasamira pakamwa pao; Anandiomba pama ndi kunditonza; Asonkhana pamodzi kunditsutsa.
11
Mulungu andipereka kwa osalungama, Nandiponya m'manja a oipa.
12
Ndinali mkupuma, koma anandityola; Inde anandigwira pakhosi, nandiphwanya; Anandiimika ndikhale candamali.
13
Eni mauta ace andizinga, Ang'amba imso zanga, osazileka; Natsanulira pansi ndulu yanga.
14
Andipasula-pasula; Andithamangira ngati wamphamvu.
15
Ndadzisokerera ciguduli ku khungu langa, Ndipo ndaipsa mphamvu yanga m'pfumbi.
16
Nkhope yanga njodetsedwa ndi kulira misozi, Ndi pa zikope zanga pali mthunzi wa imfa;
17
Pangakhale palibe ciwawa m'manja mwanga, Ndi pemphero langa ndi loyera.
18
Dziko iwe, usakwirire mwazi wanga, Ndi kulira kwanga kusowe popumira.
19
Tsopanonso, taona, mboni yanga iri kumwamba, Ndi nkhoswe yanga ikhala m'mwamba.
20
Mabwenzi anga andinyoza; Koma diso langa lilirira misozi kwa Mulungu;
21
Ha! munthu akadapembedzera mnzace kwa Mulungu, Monga munthu apembedzera mnansi wace!
22
Pakuti zitafika zaka zowerengeka, Ndidzamuka ku njira imene sindibwererako.
← Chapter 15
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 17 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42