bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 20
Job 20
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 19
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 21 →
1
Pamenepo anayankha Zofari Mnaama, nati,
2
M'mwemo zolingirira zanga zindiyankha, Cifukwa cace ndifulumidwa m'kati mwanga.
3
Ndamva kudzudzula kwakundicititsa manyazi, Ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.
4
Kodi sucidziwa ici ciyambire kale lomwe, Kuyambira anaika munthu pa dziko lapansi,
5
Kuti kupfuula kokondwera kwa woipa sikukhalira kutha, Ndi cimwemwe ca wonyoza Mulungu cikhala kamphindi?
6
Cinkana ukulu wace ukwera kumka kuthambo, Nugunda pamitambo mutu wace;
7
Koma adzatayika kosatha ngati zonyansa zace; Iwo amene adamuona adzati, Ali kuti iye?
8
Adzauluka ngati loto, osapezekanso; Nadzaingidwa ngati masomphenya a usiku.
9
Diso lidamuonalo silidzamuonanso; Ndi malo ace sadzampenyanso.
10
Ana ace adzapempha aumphawi awakomere mtima; Ndi manja ace adzabweza cuma cace.
11
Mafupa ace adzala nao unyamata wace, Koma udzagona naye pansi m'pfumbi.
12
Cinkana coipa cizuna m'kamwa mwace, Cinkana acibisa pansi pa lilime lace;
13
Cinkana acisunga, osacileka, Naoikhalitsa m'kamwa mwace;
14
Koma cakudya cace cidzasandulika m'matumbo mwace, Cidzakhala ndulu ya mphiri mkati mwace.
15
Anacimeza cuma koma adzacisanzanso; Mulungu adzaciturutsa m'mimba mwace.
16
Adzayamwa ndulu ya mphiri; Pakamwa pa njoka padzamupha.
17
Sadzapenyerera timitsinje, Toyenda nao uci ndi mafuta.
18
Cimene adagwiriraco nchito, adzacibweza, osacimeza; Sadzakondwera monga mwa zolemera zace adaziona.
19
Pakuti anapsinja, nasiya aumphawi; Analanda nyumba mwaciwawa, imene sanaimanga.
20
Popeza sanadziwa kupumula m'kati mwace, Sadzalanditsa kanthu ka zofunika zace.
21
Sikunatsalira kanthu kosadya iye, Cifukwa cace zokoma zace sizidzakhalitsa.
22
Pomkwanira kudzala kwace adzakhala m'kusauka; Dzanja la yense wobvutika lidzamgwera,
23
Poti adzaze mimba yace, Mulungu adzamponyera mkwiyo wace waukali, Nadzambvumbitsira uwu pakudya iye.
24
Adzathawa cida cacitsulo, Ndi mubvi wa uta wamkuwa udzampyoza.
25
Auzula, nuturuka m'thupi mwace; Inde nsonga yonyezimira ituruka m'ndulu mwace; Zamgwera zoopsa.
26
Zamdima zonse zimsungikira zikhale cuma cace, Moto wosaukoleza munthu udzampsereza; Udzatha wotsalira m'hema mwace.
27
M'mwamba mudzabvumbulutsa mphulupulu yace, Ndi dziko lapansi lidzamuukira.
28
Phindu la m'nyumba mwace lidzacoka, Akatundu ace adzamthawa tsiku la mkwiyo wace.
29
Ili ndi gawo la munthu woipa, locokera kwa Mulungu, Ndi colowa amuikiratu Mulungu.
← Chapter 19
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 21 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42