bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 17
Job 17
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 16
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 18 →
1
Mzimu wanga watha, masiku anga afafanizika, Kumanda kwandikonzekeratu.
2
Zoonadi, ali nane ondiseka; Ndi diso langa liri cipenyere m'kundiwindula kwao.
3
Mupatse cigwiriro tsono, mundikhalire cikole Inu nokha kwanu; Ndani adzapangana nane kundilipirira?
4
Pakuti mwabisira mtima wao nzeru; Cifukwa cace simudzawakuza.
5
Iye wakupereka mabwenzi ace kuukapolo, M'maso mwa ana ace mudzada.
6
Anandiyesanso nthanthi za anthu; Ndipo ndakhala ngati munthu womthira malobvu pankhope pace.
7
M'diso mwanga mucita cizirezire cifukwa ca cisoni, Ndi ziwalo zanga zonse ziribe cithunzi.
8
Anthu oongoka mtima adzadabwa naco, Ndi munthu wosalakwa adzadziutsa kumtsotsa wonyoza Mulunguyo.
9
Koma wolungama asungitsa njira yace, Ndi iye wa manja oyera adzakulabe mumphamvu.
10
Koma bwerani inu nonse, idzani tsono; Pakuti sindipeza mwa inu wanzeru.
11
Masiku anga apitirira, zolingirira zanga zaduka, Zace zace zomwe za mtima wanga.
12
Zisanduliza usiku ukhale usana; Kuunika kuyandikana ndi mdima.
13
Ndikayembekezera kumanda kukhale nyumba yanga; Ndikayala pogona panga mumdima.
14
Ndikati kwa dzenje, Ndiwe atate wanga; Kwa mphutsi, Ndiwe mai wanga ndi mlongo wanga;
15
Ciri kuti ciyembekezo canga? Inde, ciyembekezo canga adzaciona ndani?
16
Cidzatsikira ku mipingiridzo ya kumanda, Pamene tipumulira pamodzi kupfumbi.
← Chapter 16
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 18 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42