bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 14
Job 14
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 13
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 15 →
1
Munthu wobadwa ndi mkazi Ngwa masiku owerengeka, nakhuta mabvuto,
2
Aturuka ngati duwa, nafota; Athawa ngati mthunzi, osakhalitsa.
3
Ndipo kodi mumtsegulira maso anu wotereyo, Ndi kunditenga kunena nane mlandu Inu?
4
Adzaturutsa coyera m'cinthu codetsa ndani? nnena mmodzi yense.
5
Popeza masiku ace alembedwa, ciwerengo ca miyezi yace cikhala ndi Inu, Ndipo mwamlembera malire ace, kuti asapitirirepo iye;
6
Mumleke osamthira maso, kuti apumule, Kuti akondwere nalo tsiku lace monga wolembedwa nchito.
7
Pakuti akaulikha mtengo pali ciyembekezo kuti udzaphukanso, Ndi kuti nthambi yace yanthete siidzasowa.
8
Ngakhale muzu wace wakalamba m'nthaka, Ndi tsinde lace likufa pansi;
9
Koma pa mnunkho wa madzi udzaphuka, Nudzaswa nthambi ngati womera.
10
Koma munthu akufa atacita liondeonde Inde, munthu apereka mzimu wace, ndipo ali kuti?
11
Madzi acoka m'nyanja, Ndi mtsinje ukuphwa, nuuma;
12
Momwemo munthu agona pansi, osaukanso; Kufikira miyamba kulibe, sadzaukanso, Kapena kuutsidwa pa tulo tace.
13
Ha! mukadandibisa kumanda, Mukadandisunga m'tseri, mpaka wapita mkwiyo wanu. Mukadandiikira nthawi, ndi kundikumbukira.
14
Atafa munthu, adzakhalanso ndi moyo kodi? Ndikadayembekeza masiku onse a nkhondo yanga, Mpaka kwafika kusandulika kwanga,
15
Mukadaitana, ndipo ndikadakuyankhani; Mukadakhumba nchito ya manja anu.
16
Koma tsopano muwerenga maponda mwanga; Kodi simuyang'anitsa cimo langa?
17
Colakwa canga caikidwa m'thumba lokomedwa cizindikilo; Ndipo mumanga pamodzi mphulupulu zanga.
18
Ndipo zoonadi, likagwa phiri, latha; Ndi thanthwe lisunthika m'malo mwace;
19
Madzi anyenya miyala; Zosefukira zao zikokolola pfumbi la nthaka; Ndipo muononga ciyembekezo ca munthu.
20
Mumlaka cilakire, napita iye; Musintha nkhope yace, mumuuza acoke.
21
Ana ace aona ulemu osadziwa iye; Napeputsidwa, koma osazindikira za iwo.
22
Koma thupi lace limuwawira yekha, Ndi mtima wace umliritsa yekha.
← Chapter 13
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 15 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42