bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 5
Job 5
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 4
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 6 →
1
Itana tsono; pali wina wakukuyankha kodi? Ndipo udzatembenukira kwa yani wa oyera mtimawo?
2
Pakuti mkwiyo umapha wopusa, Ndi nsanje imakantha wopanda pace.
3
Ndinapenya wopusa woyala mizu; Koma pomwepo ndinatemberera pokhala pace.
4
Ana ace akhala otekeseka, Napsinjika kucipata, Wopanda wina wakuwapulumutsa.
5
Zokolola zao anjala azidya, Azitenga ngakhale kuminga, Ndi aludzu ameza cuma cao.
6
Pakuti nsautso siituruka m'pfumbi, Ndi mabvuto saphuka m'nthaka;
7
Koma munthu abadwira mabvuto, Monga mbaliwali zikwera ziuluzika.
8
Koma ine ndikadafuna Mulungu, Ndikadaikira mlandu wanga Mulungu;
9
Amene acita zazikuru ndi zosalondoleka, Zinthu zodabwiza zosawerengeka.
10
Amene abvumbitsa mvula panthaka, Natumiza madzi paminda;
11
Kuika opeputsidwa pamalo ponyamuka, Kuti iwo a maliro akwezedwe posatekeseka.
12
Apititsa pacabe ziwembu za ocenjerera, Kuti manja ao sakhoza kucita copangana cao.
13
Akola eni nzeru m'kucenjerera kwao, Ndi uphungu wa opotoka mtima usonthokera pacabe,
14
Iwo akomana ndi mdima pali dzuwa, Nayambasa dzuwa liri pakati pamtu monga usiku.
15
Apulumutsa aumphawi ku lopanga La kukamwa kwao, ndi ku dzanja la wamphamvu.
16
Potero aumphawi ali naco ciyembekezo, Ndi mphulupulu yatsekedwa pakamwa.
17
Taona, wodala munthu amene Mulungu amdzudzula; Cifukwa cace usapeputsa kulanga kwa Wamphamvuyonse.
18
Pakuti apweteka, namanganso mabala; Alasa, ndi manja ace omwe apoletsa.
19
Adzakupulumutsa m'masautso asanu ndi limodzi; Cinkana mwa asanu ndi awiri palibe coipa cidzakukhudza.
20
Adzakuombola kuimfa m'njala, Ndi ku mphamvu ya lupanga m'nkhondo.
21
Udzabisikira mkwapulo wa lilime, Sudzaciopanso cikadza cipasuko.
22
Cipasuko ndi njala udzaziseka; Ngakhale zirombo za padziko osaziopa.
23
Pakuti udzakhala ndi pangano ndi miyala ya kuthengo; Ndi nyama za kuthengo zidzakhala nawe mumtendere.
24
Ndipo udzapeza kuti pahema pako mpa mtendere; Nudzazonda za m'banja mwako osasowapo kanthu,
25
Udzapezanso kuti mbeu zako zidzacuruka, Ndi obala iwe ngati zitsamba za padziko.
26
Udzafika kumanda utakalamba, Monga abwera nao mtolo wa tirigu m'nyengo yace.
27
Taona, ici tacifunafuna, ciri catero; Ucimvere, nucidziwire wekha.
← Chapter 4
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 6 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42