bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 23
Job 23
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 22
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 24 →
1
Koma Yobu anayankha, nati,
2
Lero lomwe kudandaula kwanga kumawawa; Kulanga kwanga kuposa kubuula kwanga m'kulemera kwace.
3
Ha! ndikadadziwa kumene ndikampeza Mulungu, Kuti ndifike ku mpando wace!
4
Ndikadalongosola mlandu wanga pamaso pace, Ndikadadzaza m'kamwa mwanga ndi matsutsano.
5
Ndikadadziwa mau akadandiyankha ine, Ndikadazindikira cimene akadanena nane.
6
Akadatsutsana nane kodi mwa mphamvu yace yaikuru? Iai, koma akadandicherera khutu.
7
Apo woongoka mtima akadatsutsana naye; Ndipo ndikadapulumuka cipulumukire kwa Woweruza wanga.
8
Taonani, ndikamka m'tsogolo, kulibe Iye; Kapena m'mbuyo sindimzindikira;
9
Akacita Iye kulamanzere, sindimpenyerera; Akabisala kulamanja, sindimuona,
10
Koma adziwa njira ndilowayi; Atandiyesa ndidzaturuka ngati golidi.
11
Phazi langa lagwiratu moponda Iye, Ndasunga njira yace, wosapambukamo.
12
Sindinabwerera kusiya malamulo a pa milomo yace; Ndasungitsa mau a pakamwa pace koposa lamulo langa langa.
13
Koma Iye ndiye wa mtima umodzi, adzambweza ndani? Ndi ici cimene moyo wace ucifuna acicita.
14
Pakuti adzacita condiikidwiratu; Ndipo zambiri zotere ziri ndi Iye.
15
Cifukwa cace ndiopsedwa pankhope pace; Ndikalingirira, ndicita mantha ndi Iye.
16
Pakuti Mulungu walefula mtima wanga, Ndi Wamphamvuyonse wandiopsa.
17
Popeza sindinalikhidwa usanafike mdimawo, Ndipo sanandiphimbira nkhope yanga ndi mdima wa bii.
← Chapter 22
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 24 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42