bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 35
Job 35
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 34
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 36 →
1
Ndipo Elihu anabwereza kunena, nati,
2
Kodi muciyesa coyenera, Umo mukuti, Cilungamo canga ciposa ca Mulungu,
3
Pakuti munena, Upindulanji naco? Posacimwa ndinapindula ciani cimene sindikadapindula pocimwa?
4
Ndidzakuyankhani, Ndi anzanu pamodzi ndi inu.
5
Yang'anani kumwamba, nimuone, Tapenyani mitambo yokwera yakuposa inu.
6
Ngati mwacimwa, mumcitira Iye ciani? Zikacuruka zolakwa zanu, mumcitira Iye ciani?
7
Mukakhala wolungama, mumninkhapo ciani? Kapena alandira ciani pa dzanja lanu?
8
Coipa canu cikhoza kuipira munthu wonga inu, Ndi cilungamo canu cikhoza kukomera wobadwa ndi munthu.
9
Cifukwa ca kucuruka masautso anthu anapfuula, Apfuula cifukwa ca dzanja la amphamvu.
10
Koma palibe anganene, Ali kuti Mulungu Mlengi wanga, Wakupatsa nyimbo usiku;
11
Wakutilangiza ife koposa nyama za padziko, Wakutipatsa nzeru zoposa mbalame za m'mlengalenga?
12
Apo apfuula, koma Iye sawayankha; Cifukwa ca kudzikuza kwa anthu oipa.
13
Zedi Mulungu samvera zacabe, Ndi Wamphamvuyonse sazisamalira.
14
Inde mungakhale munena, Sindimpenya, Mlanduwo uli pamaso pace, ndipo mumlindira.
15
Ndipo tsopano popeza analibe kumzonda m'kukwiya kwace, Ndi kusamalitsa colakwa,
16
Cifukwa cace Yobu anatsegula pakamwa pace mwacabe, Nacurukitsa mau opanda nzeru.
← Chapter 34
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 36 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42