bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 41
Job 41
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 40
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 42 →
1
Kodi ukhoza kukoka ng'ona ndi mbedza? Kapena kukanikiza kalandira wace ndi cingwe?
2
Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wace ndi momba?
3
Kodi idzacurukitsa mau akukupembedza? Kapena idzanena nawe mau ofatsa?
4
Kodi idzapangana ndi iwe, Kuti uitenge ikhale kapolo wako wacikhalire?
5
Kodi udzasewera nayo ngati mbalame? Kapena udzaimangira anamwali ako kuti aiwete?
6
Kodi opangana malonda adzaitsatsa? Adzaigawana eni malonda?
7
Kodi udzadzaza khungu lace ndi nchetho, Kapena mutu wace ndi miomba?
8
Isanjike dzanja lako; Ukakumbukila nkhondoyi, sudzateronso.
9
Taona, ciyembekezo cako ca pa iyo cipita pacabe. Kodi sadzatenga nkhawa munthu pakungoiona?
10
Palibe wolimba mtima kuti adzaiputa. Ndipo ndaniyo adzaima pamaso pa Ine?
11
Ndaniyo anayamba kundipatsa Ine kuti ndimthokoze? Ziri zonse pansi pa thambo ponse ndi zanga.
12
Sindikhala cete osachula ziwalo za ng'onayo, Ndi mbiri ya mphamvu yace, ndi makonzedwe ace okoma.
13
Ndani adzasenda cobvala cace cakunja? Adzalowa ndani ku mizere iwiri ya mano ace?
14
Adzatsegula ndani zitseko za pakamwa pace? Mano ace aopsa pozungulira pao.
15
Maamba ace olimba ndiwo kudzitama kwace; Amangika pamodzi ngati okomeredwatu.
16
Alumikizana lina ndi linzace, Mphepo yosalowa pakati pao.
17
Amamatirana lina ndi linzace, Agwirana osagawanikana.
18
Pakuyetsemula ing'anipitsa kuunika, Ndi maso ace akunga zikope za m'mawa.
19
M'kamwa mwace muturuka miuni, Mbaliwali za moto zibukamo.
20
M'mphuno mwace muturuka utsi, Ngati nkhali yobwadamuka ndi moto wa zinyatsi.
21
Mpweya wace uyatsa makara, Ndi m'kamwa mwace muturuka lawi la moto.
22
Kukhosi kwace kukhala mphamvu, Ndi mantha abvumbuluka patsogolo pace,
23
Nyama yace yopsapsala igwirana Ikwima pathupi pace yosagwedezeka.
24
Mtima wace ulimba ngati mwala, Inde ulimba ngati mwala wa mphero,
25
Ikanyamuka, amphamvu acita mantha; Cifukwa ca kuopsedwa azimidwa nzeru.
26
Munthu akaiyamba ndi lupanga, ligoma; Ngakhale nthungo, kapena mubvi, kapena mkondo.
27
Citsulo iciyesa phesi, Ndi mkuwa ngati mtengo woola.
28
Mubvi suithawitsa, Miyala ya pacoponyera iisandutsa ciputu,
29
Zibonga ziyesedwa ciputu, Iseka kuthikuza kwace kwa nthungo,
30
Kumimba kwace ikunga mapale akuthwa, Itasalala kuthope ngati copunthira.
31
Icititsa nthubwinthubwi pozama ngati nkhali, Isanduliza nyanja ikunge mafuta.
32
Icititsa mifunde yonyezimira pambuyo pace; Munthu akadati pozama pali ndi imvi.
33
Pa dziko lapansi palibe cina colingana nayo, Colengedwa copanda mantha.
34
Ipenya ciri conse codzikuza, Ndiyo mfumu ya zodzitama zonse.
← Chapter 40
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 42 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42