bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 40
Job 40
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 39
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 41 →
1
Ndipo Yehova anabwereza kwa Yobu, nati,
2
Kodi wodzudzulayo atsutsane ndi Wamphamvuyonse? Wocita makani ndi Mulungu ayankhe.
3
Pamenepo Yobu anayankha Yehova, nati,
4
Taonani, ndakhululuka ine, ndidzakubwezerani mau otani? Ndigwira pakamwa.
5
Ndalankhula kamodzi, koma sindidzayankha; Inde kawiri, koma sindionjezanso.
6
Ndipo Yehova anamyankha Yobu m'kabvumvulu, nati,
7
Dzimangire m'cuuno tsono ngati mwamuna; Ndidzakufunsa, undidziwitse.
8
Cingakhale ciweruzo canga udzacityola kodi? Udzanditsutsa kuti ndiri woipa kodi, kuti ukhale wolungama ndiwe?
9
Kodi uli nalo dzanja ngati Ine Mulungu? Kapena ukhoza kugunda ndi mau ngati Ine?
10
Udzikometsere tsono ndi ukulu ndi kukuzika, Nubvale ulemu ndi ulemerero.
11
Tsanulira mkwiyo wako wosefuka, Nupenyerere ali yense wodzikuza ndi kumcepetsa,
12
Upenyerere ali yense wodzikuza, numtsitse, Nupondereze oipa pomwe akhala.
13
Uwakwirire pamodzi m'pfumbi, Uzimange nkhope zao pobisika.
14
Pamenepo inenso ndidzakubvomereza, Kuti dzanja lako lako lamanja likupulumutsa.
15
Tapenya tsono mvuu ndinaipanga pamodzi ndi iwe, Ikudya udzu ngati ng'ombe.
16
Tapenya tsono, mphamvu yace iri m'cuuno mwace, Ndi kulimbalimba kwace kuli m'mitsempha ya m'mimba yace.
17
Igwedeza mcira wace ngati mkungudza; Mitsempha ya ncafu zace ipotana.
18
Mafupa ace akunga misiwe yamkuwa; Ziwalo zace zikunga zitsulo zamphumphu,
19
Iyo ndiyo ciyambi ca macitidwe a Mulungu; Wakuilenga anaininkha lupanga lace.
20
Pakuti mapiri aiphukitsira cakudya, Kumene zisewera nyama zonse za kuthengo,
21
Igona pansi patsinde pa mitengo yamthunzi, Pobisala pabango ndi pathawale.
22
Mitengo yamthunzi iiphimba ndi mthunzi wao, Misondodzi ya kumtsinje iizinga.
23
Taona madzi a mumtsinje akakula, siinjenjemera; Ilimbika mtima, ngakhale Yordano atupa mpaka pakamwa pace,
24
Ikakhala maso, munthu adzaigwira kodi? Kapena kuboola m'mphuno mwace iri m'khwekhwe?
← Chapter 39
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 41 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42