bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 7
Job 7
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 6
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 8 →
1
Kodi munthu alibe nkhondo kunja kuno? Kodi masiku ace sakunga masiku a wolembedwa nchito?
2
Monga kapolo woliralira mthunzi, Monga wolembedwa nchito ayembekezera mphotho yace,
3
Momwemo anandilowetsa miyezi yopanda pace. Nandiikiratu zowawa usiku ndi usiku.
4
Ndigona pansi, ndikuti, Ndidzauka liti? koma usiku undikulira; Ndipo ndimapalapata mpaka mbanda kuca.
5
Mnofu wanga wabvala mphutsi ndi nkanambo zadothi; Khungu langa lang'ambika, nilinyansa.
6
Masiku anga afulumira koposa mphindo ya muomba, Apitirira opanda ciyembekezo.
7
Kumbukila kuti moyo wanga ndiwo mphepo, Diso langa silidzaonanso cokoma.
8
Diso la amene andiona silidzandionanso, Maso ako adzandipenyetsetsa, koma ine palibe.
9
Mtambo wapita watha, Momwemo wakutsikira kumanda sadzakwerakonso.
10
Sadzabweranso ku nyumba yace, Osamdziwanso malo ace.
11
Potero sindidzaletsa pakamwa panga; Ndidzalankhula popsinjika mumzimu mwanga; Ndidzadandaula pakuwawa mtima wanga.
12
Ndine nyanja kodi, kapena cinjoka ca m'nyanja, Kuti Inu mundiikira odikira?
13
Ndikati, Pakama panga mpondisangalatsa, Pogona panga padzacepsa condidandaulitsa;
14
Pamenepo mundiopsa ndi maloto, Nimundicititsa mantha ndi masomphenya;
15
Potero moyo wanga usankha kupotedwa, Ndi imfa, koposa mafupa anga awa.
16
Ndinyansidwa nao moyo wanga; sindidzakhala ndi moyo cikhalire; Mundileke; pakuti masiku anga ndi acabe.
17
Munthu ndani kuti mumkuze, Ndi kuti muike mtima wanu pa iye,
18
Ndi kuti muceze naye m'mawa ndi m'mawa, Ndi kumuyesa nthawi zonse?
19
Mukana kundicokera kufikira liti, Kapena kundileka mpaka nditameza dobvu?
20
Ngati ndacimwa, ndingacitire Inu ciani, Inu wodikira anthu? Mwandiikiranji ndikhale candamali canu? Kuti ndikhale kwa ine ndekha katundu?
21
Mulekeranji kukhululukira kulakwa kwanga ndi kundicotsera mphulupulu yanga? Popeza tsopano ndidzagona kupfumbi; Mudzandifunafuna, koma ine palibe.
← Chapter 6
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 8 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42