bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 33
Job 33
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 32
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 34 →
1
Komatu, Yobu, mumvere maneno anga, Mucherere khutu mau anga.
2
Taonani tsono, ndatsegula pakamwa panga, Lilime langa lanena m'kamwa mwanga.
3
Maneno anga aulula ciongoko ca mtima wanga, Ndi monga umo idziwira milomo yanga idzanena zoona.
4
Mzimu wa Mulungu unandilenga, Ndi mpweya wa Wamphamvuyonse umandipatsa moyo.
5
Ngati mukhoza, mundiyankhe; Mulongosolere mau anu pamaso panga, mukonzeke.
6
Taonani, ndikhala kwa Mulungu ngati inu; Inenso ndinaumbidwa ndi dothi,
7
Taonani, kuopsa kwanga simudzacita nako mantha; Ndi ici ndikusenzetsani sicidzakulemererani.
8
Zedi mwanena m'makutu mwanga, Ndinamvanso mau akunena kwanu, akuti,
9
Ndine woyera ine, wopanda kulakwa, Ndine wosaparamula, ndiribe mphulupulu.
10
Taonani, Iye apeza zifukwa zoti anditsutse nazo, Andiyesa mdani wace;
11
Amanga mapazi anga m'zigologolo, Ayang'anira poyenda ine ponse.
12
Taonani, ndidzakuyankhani m'mene muli mosalungama; Pakuti Mulungu ndiye wamkulu woposa munthu.
13
Mutsutsana ndi Iye cifukwa ninji? Popeza pa zace zonse saulula cifukwa.
14
Pakuti Mulungu alankhula kamodzi, Kapena kawiri, koma anthu sasamalira.
15
M'kulota, m'masomphenya a usiku, Pakuwagwera anthu tulo tatikuru, Pogona mwacheru pakama,
16
Pamenepo atsegula makutu a anthu, Nakomera cizindikilo cilangizo cao;
17
Kuti acotse munthu ku cimene akadacita, Ndi kubisira munthu kudzikuza kwace;
18
Kuti amletse angaonongeke, Ndi moyo wace ungatayike ndi lupanga.
19
Alangidwanso ndi zowawa pakama pace, Ndi kulimbana kowawa kosapuma m'mafupa ace.
20
M'mwemo mtima wace ucita mseru ndi mkate, Ndi moyo wace pa cakudya colongosoka.
21
Mnofu wace udatha, kuti sungapenyeke; Ndi mafupa ace akusaoneka aturuka.
22
Inde wasendera kufupi ku manda, Ndi moyo wace kwa akuononga.
23
Akakhala kwa iye mthenga, Womasulira mau mmodzi mwa cikwi, Kuonetsera munthu comuyenera;
24
Pamenepo Mulungu amcitira cifundo, nati, Mlanditse, angatsikire kumanda, Ndampezera dipo.
25
Mnofu wace udzakhala se, woposa wa mwana; Adzabwerera ku masiku a ubwana wace.
26
Apembedza Mulungu, ndipo amkomera mtima; M'mwemo aona nkhope yace mokondwera; Ndipo ambwezera munthu cilungamo cace.
27
Apenyerera anthu, ndi kuti, Ndinacimwa, ndaipsa coongokaco, Ndipo sindinapindula nako.
28
Koma anandiombola ndingatsikire kumanda, Ndi moyo wanga udzaona kuunika.
29
Taona, izi zonse azicita Mulungu Kawiri katatu ndi munthu,
30
Kumbweza angalowe kumanda, Kuti kuunika kwa moyo kumuwalire.
31
Cherani khutu, Yobu, mundimvere ine; Mukhale cete, ndipo ndidzanena ine.
32
Ngati muli nao mau mundiyankhe. Nenani, pakuti ndifuna kukulungamitsani.
33
Ngati mulibe mau, tamverani Ine; Mukhale cete, ndipo ndizakuphunzitsani nzeru.
← Chapter 32
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 34 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42