bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 8
Job 8
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 7
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 9 →
1
Pamenepo anayankha Bilidadi Msuki, nati,
2
Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati namondwe kufikira liti?
3
Ngati Mulungu akhotetsa ciweruzo? Ngati Wamphamvuyonse akhotetsa mlandu?
4
Cinkana ana ako anamcimwira Iye, Ndipo anawapereka mwa kulakwa kwao;
5
Koma ukafunitsitsa Mulungu, Ndi kupembedza Wamphamvuyonse;
6
Ukakhala woyera ndi woongoka mtima, Zoonadi adzakugalamukira tsopano, Ndi kupindulitsa pokhala pako polungama.
7
Ndipo cinkana ciyambi cako cinali cacing'ono, Citsiriziro cako cidzacuruka kwambiri.
8
Pakuti ufunsire tsono mbadwo wapitawo, Nusamalire zimene makolo ao adazisanthula;
9
Pakuti ife ndife adzulo, osadziwa kanthu, Popeza masiku athu a pa dziko lapansi ndiwo ngati mthunzi;
10
Amene aja sangakuphunzitse, ndi kukufotokozera, Ndi kuturutsa mau a mumtima mwao?
11
Ngati gumbwa aphuka popanda cinyontho? Ngati mancedza amera popanda madzi?
12
Akali auwisi, sanawaceka, Auma, asanaume mathengo onse ena.
13
Momwemo mayendedwe a onse oiwala Mulungu; Ndi ciyembekezo ca onyoza Mulungu cidzatayika;
14
Kulimbika mtima kwace kudzatyoka, Cikhulupiriro cace cikunga nyumba ya tandaude.
15
Adzatsamira nyumba yace, koma yosamlimbira; Adzaiumirira koma yosakhalitsa.
16
Akhala wamuwisi pali dzuwa, Ndi nthambi zace ziturukira pamunda pace.
17
Mizu yace iyangayanga pa kasupe wamadzi, Apenyerera pokhalapo miyala.
18
Akamuononga kumcotsa pamalo pace, Padzamkana, ndi kuti, Sindinakuona.
19
Taona, ici ndico comkondweretsa panjira pace, Ndi panthaka padzamera ena.
20
Taona, Mulungu sakana munthu wangwiro; Kapena kugwiriziza ocita zoipa.
21
Koma adzadzaza m'kamwa mwako ndi kuseka, Ndi milomo yako kupfuula.
22
Iwo akudana nawe adzabvala manyazi; Ndi hema wa oipa adzakhala kuli zi.
← Chapter 7
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 9 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42