bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Job 27
Job 27
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 26
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 28 →
1
Ndipo Yobu anaonjezanso mwambi wace, nati,
2
Pali Mulungu, amene anandicotsera zoyenera ine, Ndi Wamphamvuyonse, amene anawawitsa moyo wanga,
3
Pakuti moyo wanga wonse ukali mwa ine, Ndi mpweya wa Mulungu m'mphuno mwanga;
4
Milomo yanga siilankhula cosalungama, Ndi lilime langa silichula zacinyengo.
5
Sindibvomereza konse kuti muli olungama; Mpaka kufa ine sinditaya ungwiro wanga.
6
Ndiumirira cilungamo canga, osacileka; Cikhalire moyo ine, mtima wanga sunditonza.
7
Mdani wanga akhale ngati woipa, Ndi iye amene andiukira ngati wosalungama.
8
Pakuti ciyembekezo ca wonyoza Mulungu nciani pomlikhatu Mulungu, Pomcotsera moyo wace?
9
Kodi Mulungu adzamvera kupfuula kwace, ikamdzera nsautso?
10
Kodi adzadzikondweretsa naze Wamphamvuyonse, Ndi kuitana kwa Mulungu nthawi zonse?
11
Ndidzakulangizani za dzanja la Mulungu; Cokhala ndi Wamphamvuyonse sindidzacibisa.
12
Taonani, inu nonse munaciona; Ndipo mugwidwa nazo zopanda pace cifukwa ninji?
13
Ili ndi gawo la munthu woipa kwa Mulungu, Ndi colowa ca akupsinja anzao acilandira kwa Wamphamvtiyonse.
14
Akacuruka ana ace, ndiko kucurukira lupanga, Ndi ana ace sadzakhuta cakudya.
15
Akumtsalira iye adzaikidwa muimfa, Ndi akazi ace amasiye sadzalira maliro.
16
Cinkana akundika ndalama ngati pfumbi, Ndi kukonzeratu zobvala ngati dothi;
17
Azikonzeretu, koma wolungama adzazibvala, Ndi wosalakwa adzagawa ndalamazo.
18
Amanga nyumba yace ngati kadzoce, Ndi ngati wolindira amanga dindiro.
19
Agona pansi ali wacuma, koma saikidwa; Potsegula maso ace, wafa cikomo,
20
Zoopsa zimgwera ngati madzi; Nkuntho umtenga usiku.
21
Mphepo ya kum'mawa Imtenga, nacokaiye; Nimkankha acoke m'malo mwace.
22
Pakuti Mulungu adzamponyera zoopsa, osanlieka; Kuthawa akadathawa m'dzanja lace.
23
Anthu adzamuombera manja, Nadzamuyimbira mluzu acoke m'malo mwace.
← Chapter 26
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 28 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42