bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
1 Chronicles 8
1 Chronicles 8
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 7
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 9 →
1
Benjamini adabereka Bela mwana wake wachisamba, Asibele mwana wake wachiŵiri, Ahara mwana wake wachitatu,
2
Noha mwana wake wachinai ndi Rafa mwana wake wachisanu.
3
Bela anali ndi zidzukulu izi: Adara, Gera, Abihudi,
4
Abisuwa, Namani, Ahowa,
5
Gera, Sefufani ndiponso Huramu.
6
Ana a Ehudi amene anali atsogoleri a mabanja okhala ku Geba, adachotsedwa kwaoko ndipo adakakhala ku Manahati.
7
Anawo anali Namani, Ahiya ndi Gera. Gerayo amene anali bambo wake wa Uza ndi Ahihudi, ndiye adatsogolera anthu osamutsidwawo.
8
Saharaimu, atachotsa akazi ake Husimu ndi Baara, adakhala ndi ana m'dziko la Mowabu.
9
Mwa mkazi wake Hodesi adabelekamo ana aŵa: Yobabu, Zibiya, Mesa, Malikamu,
10
Yeuzi, Sakiya ndi Mirima. Ameneŵa ndiwo amene anali ana ake, atsogoleri a mabanja.
11
Mwa Husimu adaberekamonso ana aŵa: Abitubu, ndi Elipaala.
12
Ana a Elipaala naŵa: Ebere, Misamu ndi Semedi. Semedi ndiye adamanga mizinda ya Ono ndi Lodi pamodzi ndi midzi yake yomwe.
13
Beriya ndi Sema anali atsogoleri a mabanja okhala ku mzinda wa Aiyaloni. Iwowo adathaŵitsa nzika za ku Gati.
14
Zidzukulu zina za Beriya zinali Ahiyo, Sasaki, Yeremoti,
15
Zebadiya, Aradi, Edere,
16
Mikaele, Isipa ndi Yoha.
17
Zebadiya, Mesulamu, Hiziki, Hebere,
18
Isimerai, Iziliya ndi Yobabu anali zidzukulu za Elipaala.
19
Yakimu, Zikiri, Zabidi,
20
Eliyenai, Ziletai, Eliyele,
21
Adaya, Beraya ndi Simiratu anali zidzukulu za Simei.
22
Isipani, Ebere, Eliyele,
23
Abidoni, Zikiri, Hanani,
24
Hananiya, Elamu, Anitotiya,
25
Ifidea ndi Penuwele, anali zidzukulu za Sasaki.
26
Samuserai, Sehariya, Ataliya,
27
Yaaresiya, Eliya ndi Zikiri anali zidzukulu za Yerohamu.
28
Ameneŵa ndiwo amene anali atsogoleri a mabanja, anthu otchuka potsata mibadwo yao, ndipo onsewo ankakhala ku Yerusalemu.
29
Yeiyele, amene adaamanga Gibiyoni, ankakhala ku Gibiyoni komweko. Mkazi wake anali Maaka.
30
Mwana wake wachisamba anali Abidoni, pambuyo pa iyeyo panali Zuri, Kisi, Baala, Nere, Nadabu,
31
Gedori, Ahiyo, Zekeri,
32
ndi Mikiloti bambo wa Simea). Tsono, monga achibale ao aja, iwoŵanso ankakhala ku Yerusalemu pamodzi ndi achibale aowo.
33
Nere adabereka Kisi, Kisi adabereka Mfumu Saulo, Mfumu Saulo adabereka Yonatani, Malikisuwa, Abinadabu, ndi Esibaala.
34
Yonatani adabereka Meribaala. Meribaala adabereka Mika.
35
Ana a Mika naŵa: Pitoni, Meleki, Tareya ndi Ahazi.
36
Ahazi adabereka Yehoyada, Yehoyada adabereka Alemeti, Azimaveti ndi Zimiri. Zimiri adabereka Moza,
37
Moza adabereka Bineya, Bineya adabereka Rafa, Rafa adabereka Eleasa, Eleasa adabereka Azele.
38
Azele anali ndi ana asanu ndi mmodzi, ndipo maina ao naŵa: Azirikamu, Bokeru, Ismaele, Seyariya, Obadiya ndi Hanani. Onseŵa anali ana a Azele.
39
Ana a mbale wake Eseki naŵa: mwana wake wachisamba Ulamu, wachiŵiri Yeusi, wachitatu Elifeleti.
40
Ana a Ulamu anali ankhondo amphamvu, anthu amauta, ndipo anali ndi ana ndi adzikulu 150. Onseŵa anali Abenjamini.
← Chapter 7
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 9 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29