bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 13
Proverbs 13
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 12
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 14 →
1
Mwana wanzeru amamvera mwambo wa atate; Koma wonyoza samvera cidzudzulo.
2
Munthu adzadya zabwino ndi zipatso za m'kamwa mwace; Koma moyo wa aciwembu udzadya ciwawa.
3
Wogwira pakamwa pace asunga moyo wace; Koma woyasamula milomo yace adzaonongeka.
4
Moyo wa wolesi ukhumba osalandira kanthu; Koma moyo wa akhama udzalemera.
5
Wolungama ada mau onama; Koma woipa anyansa, nadzicititsa manyazi,
6
Cilungamo cicinjiriza woongoka m'njira; Koma udio ugwetsa wocimwa.
7
Alipo wodziyesa wolemera, koma alibe kanthu; Alipo wodziyesa wosauka, koma ali ndi cuma cambiri.
8
Ciombolo ca moyo wa munthu ndico cuma cace; Koma wosauka samva cidzudzulo.
9
Kuunika kwa olungama kukondwa; Koma nyali ya oipa idzazima.
10
Kudzikuza kupikisanitsa; Koma omwe anauzidwa uphungu ali ndi nzeru.
11
Cuma colandiridwa mokangaza cidzacepa; Koma wokundika ndi dzanja adzaona zocuruka.
12
Ciyembekezo cozengereza cidwalitsa mtima; Koma pakufika cifuniroco ndico mtengo wa moyo.
13
Wonyoza mau adziononga yekha; Koma woopa malangizo adzalandira mphotho.
14
Malamulo a wanzeru ndiwo kasupe wa moyo, Apatutsa ku misampha ya imfa.
15
Nzeru yabwino ipatsa cisomo; Koma njira ya aciwembu iri makolokoto.
16
Yense wocenjera amacita mwanzeru: Koma wopusa aonetsa utsiru.
17
Mthenga wolakwa umagwa m'zoipa; Koma mtumiki wokhulupirika alamitsa.
18
Wokana mwambo adzasauka nanyozedwa; Koma wolabadira cidzudzulo adzalemekezedwa.
19
Cifuniro cikondweretsa moyo citacitidwa; Koma kusiya zoipa kunyansa opusa,
20
Ukayenda ndi anzeru udzakhala wanzeru: Koma mnzao wa opusa adzaphwetekedwa.
21
Zoipa zilondola ocimwa; Koma olungama adzalandira mphotho yabwino.
22
Wabwino asiyira zidzukulu zace colowa cabwino; Koma wocimwa angosungira wolungama cuma cace.
23
M'kulima kwa osauka muli zakudya zambiri; Koma zinazo zimaonongeka posowa ciweruzo.
24
Wolekereramwanace osammenya amuda; Koma womkonda amyambize kumlanga.
25
Wolungama adya nakhutitsa moyo wace; Koma mimba ya oipa idzasowa.
← Chapter 12
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 14 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31