bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 22
Proverbs 22
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 21
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 23 →
1
Mbiri yabwino ifunika kopambana cuma cambiri; Kukukomera mtima anzako kuposa siliva ndi golidi.
2
Wolemera ndi wosauka akumana, Wolenga onsewo ndiye Yehova.
3
Wocenjera aona zoipa, nabisala; Koma acibwana angopitirira, nalipitsidwa.
4
Mphotho ya cifatso ndi kuopa, Yehova Ndiye cuma, ndi ulemu, ndi moyo.
5
Minga ndi misampha iri m'njira ya wokhota; Koma wosunga moyo wace adzatarikira imeneyo.
6
Phunzitsa mwana poyamba njira yace; Ndipo angakhale atakalamba sadzacokamo.
7
Wolemera alamulira osauka; Ndipo wokongola ndiye kapolo wa womkongoletsa.
8
Wofesa zosalungama adzakolola tsoka; Ndipo ntyole ya mkwiyo wace idzalephera.
9
Mwini diso lamataya adzadala; Pakuti apatsa osauka zakudya zace.
10
Ukainga wonyoza, makangano adzaturuka; Makani ndi manyazi adzalekeka.
11
Wokonda kuyera mtima, Mfumu idzakhala bwenzi lace cifukwa ca cisomo ca milomo yace.
12
Maso a Yehova acinjiriza wodziwa; Koma agwetsa mau a munthu wa ziwembu.
13
Waulesi ati, Pali mkango panjapo, Ndidzaphedwa pamakwalalapo.
14
M'kamwa mwa mkazi waciwerewere muli dzenje lakuya; Yemwe Yehova amkwiyira adzagwamo.
15
Utsiru umangidwa mumtima mwa mwana; Koma ntyole yomlangira idzauingitsira kutari.
16
Wotsendereza waumphawi kuti acurukitse cuma cace, Ndi wopatsa wolemera kanthu, angosauka.
17
Chera makutu ako, numvere mau a anzeru, Nulozetse mtima wako kukadziwa zanga.
18
Pakuti mauwo akondweretsa ngati uwasunga m'kati mwako, Ngati akhazikika pamodzi pa milomo yako.
19
Ndakudziwitsa amenewo lero, ngakhale iwedi, Kuti ukhulupirire Yehova.
20
Kodi sindinakulembera zoposa Za uphungu ndi nzeru;
21
Kuti ukadziwitse ntheradi yace ya mau oona, Nukabwere ndi mau oona kwa iwo amene anakutumiza?
22
Usalande za waumphawi cifukwa ali waumphawi, Ngakhale kutsendereza wosauka kubwalo.
23
Pakuti Yehova adzanenera mlandu wao; Omwe akwatula zao Iye adzakwatula moyo wao.
24
Usayanjane ndi munthu wokwiya msanga; Ngakhale kupita ndi mwamuna waukali;
25
Kuti ungaphunzire mayendedwe ace, Ndi kutengera moyo wako msampha,
26
Usakhale wodulirana mpherere, Ngakhale kumperekera cikole ca ngongole zace.
27
Ngati ulibe cobwezera Kodi acotserenji kama lako pansi pako?
28
Usasunthe cidziwitso cakale ca m'malire, Cimene makolo ako anaciimika.
29
Kodi upenya munthu wofulumiza nchito zace? Adzaima pamaso pa mafumu, osaima pamaso pa anthu acabe.
← Chapter 21
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 23 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31