bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 20
Proverbs 20
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 19
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 21 →
1
Vinyo acita ciphwete, cakumwa caukali cisokosa; Wosocera nazo alibe nzeru.
2
Kuopsya kwa mfumu ndiko kubangula kwa mkango; Womputa acimwira moyo wace wace.
3
Kuli ulemu kwa mwamuna kupewa ndeu; Koma zitsiru zonse zimangokangana,
4
Wolesi salima cifukwa ca cisanu; Adzapemphapempha m'masika osalandira kanthu.
5
Uphungu wa m'mtima mwa munthu ndiwo madzi akuya; Koma munthu wozindikira adzatungapo,
6
Anthu ambiri abukitsa yense kukoma mtima kwace; Koma ndani angapeze munthu wokhulupirika?
7
Wolungama woyenda mwangwiro, Anace adala pambuyo pace.
8
Mfumu yokhala pa mpando waweruzira Ipitikitsa zoipa zonse ndi maso ace.
9
Ndani anganene, Ndasambitsa mtima wanga, Ndayera opanda cimo?
10
Miyeso yosiyana, ndi malicero osiyana, Zonse ziwirizi zinyansa Yehova.
11
Ngakhale mwana adziwika ndi nchito zace; Ngati nchito yace iri yoyera ngakhale yolungama.
12
Khutu lakumva, ndi diso lopenya, Yehova anapanga onse awiriwo.
13
Usakonde tulo ungasauke; Phenyula maso, udzakhuta zakudya.
14
Wogula ati, Cacabe cimeneco. Koma atacoka adzitama.
15
Alipo golidi ndi ngale zambiri; Koma milomo yodziwa ndiyo cokometsera ca mtengo wapatari.
16
Tenga maraya a woperekera mlendo cikole; Woperekera mkazi wacilendo cikole umgwire mwini.
17
Zakudya za cinyengo zikondweretsa munthu; Koma pambuyo pace m'kamwa mwace mudzadzala tinsangalabwi.
18
Uphungu utsimikiza zolingalira, Ponya nkhondo utapanga upo.
19
Kazitape woyendayenda awanditsa zinsinsi; Usadudukire woyasama milomo yace.
20
Wotemberera atate wace ndi, amace, Nyali yace idzazima mu mdima woti bi.
21
Colowa cingalandiridwe msanga msanga poyamba pace; Koma citsiriziro cace sicidzadala.
22
Usanene, Ndidzabwezera zoipa; Yembekeza Yehova, adzakupulumutsa.
23
Miyeso yosiyana inyansa Yehova, Ndi mulingo wonyenga suli wabwino.
24
Yehova alongosola mayendedwe a mwamuna; Munthu tsono angazindikire bwanji njira yace?
25
Kunena mwansontho, ici ncopatulika, kuli msampha kwa munthu, Ndi kusinkhasinkha pambuyo pace atawinda.
26
Mfumu yanzeru ipeta amphulupulu, Niyendetsapo njinga ya gareta.
27
Mzimu wa munthu ndiwo nyali ya Yehova; Usanthula m'kati monse mwa mimba.
28
Cifundo ndi ntheradi zisunga mfumu; Cifundo cicirikiza mpando wace.
29
Ulemerero wa anyamata ndiwo mphamvu yao; Kukongola kwa nkhalamba ndi
30
Mikwingwirima yopweteka icotsa zoipa; Ndi mikwapulo ilowa m'kati mwa mimba.
← Chapter 19
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 21 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31