bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 27
Proverbs 27
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 26
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 28 →
1
Usanyadire zamawa, Popeza sudziwa tsiku lina lidzabala ciani?
2
Wina akutame, si m'kamwamwako ai; Mlendo, si milomo ya iwe wekha.
3
Mwala ulemera, mcenga ndiwo katundu; Koma mkwiyo wa citsiru upambana kulemera kwace.
4
Kupweteka mtima nkwa nkhanza, mkwiyo usefuka; Koma ndani angalakike ndi nsanje?
5
Cidzudzulo comveka ciposa cikondi cobisika.
6
Kulasa kwa bwenzi kulikokhulupirika; Koma mdani apsompsona kawiri kawiri.
7
Mtima wokhuta upondereza cisa ca uci; Koma wakumva njala ayesa zowawa zonse zotsekemera.
8
Monga mbalame yosocera ku cisa cace, Momwemo munthu wosocera ku malo ace.
9
Mafuta ndi zonunkhira zikondweretsa mtima, Ndi ubwino wa bwenzi uteronso pakupangira uphungu,
10
Mnzako, ndi mnzace wa atate wako, usawasiye; Usanke ku nyumba ya mbale wako tsiku la tsoka lako; Mnansi wapafupi aposa mbale wakutari.
11
Mwananga, khala wanzeru, nukondweretse mtima wanga; Kuti ndimuyankhe yemwe anditonza.
12
Wocenjera aona zoipa, nabisala; Koma acibwana angopitirira, nalipitsidwa.
13
Tenga maraya a woperekera mlendo cikole; Woperekera mkazi waciwerewere cikole umgwire mwini.
14
Yemwe adalitsa mnzace ndi mau akuru pouka mamawa, Anthu adzaciyesa cimeneco temberero.
15
Kudonthadontha tsiku lamvula, Ndi mkazi wolongolola ali amodzimodzi.
16
Wofuna kumletsayo afuna kuletsa mphepo; Dzanja lace lamanja lingogwira mafuta.
17
Citsulo cinola citsulo; Comweco munthu anola nkhope ya mnzace.
18
Wosunga mkuyu adzadya zipatso zace; Wosamalira ambuyace adzalemekezedwa.
19
Monga m'madzi nkhope zionana, Momwemo mitima ya anthu idziwana.
20
Kunsi kwa manda ndi kucionongeko sikukhuta; Ngakhale maso a munthu sakhutai.
21
Siliva asungunuka m'mbiya, Ndi golidi m'ng'anjo, Motero comwe munthu acitama adziwika naco.
22
Ungakhaleukonolacitsirum'mtondo ndi munsi, pamodzi ndi mphale, Koma utsiru wace sudzamcoka.
23
Udziwitsitse zoweta zako ziri bwanji, Samalira magulu ako;
24
Pakuti cuma siciri cosatha; Kodi korona alipobe mpaka mibadwo mibadwo?
25
Amatuta maudzu, msipu uoneka, Achera masamba a kumapiri,
26
Ana a nkhosa akubveka, Atonde aombolera munda;
27
Mkaka wa mbuzi udzakukwanira kudya; Ndi a pa banja lako ndi adzakazi ako.
← Chapter 26
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 28 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31