bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 24
Proverbs 24
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 23
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 25 →
1
Usacitire nsanje anthu oipa, Ngakhale kufuna kukhala nao;
2
Pakuti mtima wao ulingalira za cionongeko; Milomo yao ilankhula za mphulupulu.
3
Nzeru imangitsa nyumba; Luntha liikhazikitsa.
4
Kudziwa kudzaza zipinda zace Ndi cuma conse cofunika ca mtengo wace.
5
Mwamuna wanzeru ngwamphamvu; Munthu wodziwa ankabe nalimba.
6
Pakuti udzaponya nkhondo yako ndi upo, Ndi kupulumuka pocuruka aphungu,
7
Nzeru itarikira citsiru; Satsegula pakamwa kubwalo.
8
Wolingalira zakucita zoipa Anthu adzamcha waciwembu.
9
Maganizo opusa ndiwo cimo; Wonyoza anyansa anthu.
10
Ukalefuka tsiku la tsoka Mphamvu yako icepa.
11
Omwe atengedwa kuti akafe, uwapulumutse; Omwe ati aphedwe, usaleke kuwalanditsa.
12
Ukanena, Taonani, sitinadziwa cimeneci; Kodi woyesa mitima sacizindikira ici? Ndi wosunga moyo wako kodi sacidziwa? Ndipo kodi sabwezera munthu yense monga mwa macitidwe ace?
13
Mwananga, idya uci pakuti ngwabwino, Ndi cisa cace citsekemera m'kamwamwako;
14
Potero udzadziwa kuti nzeru iri yotero m'moyo wako; Ngati waipeza padzakhala mphotho, Ndipo ciyembekezo cako sicidzalephereka.
15
Usabisalire, woipa iwe, pomanga wolungama; Usapasule popuma iyepo.
16
Pakuti wolungama amagwa kasanu ndi kawiri, nanyamukanso; Koma oipa akhumudwa pomfikira tsoka.
17
Usakondwere pakugwa mdani wako; Mtima wako usasekere pokhumudwa iye;
18
Kuti Yehova angaone kukondwa kwako, ndi kukuyesa koipa, Ndi kuleka kumkwiyira.
19
Usabvutike mtima cifukwa ca ocita zoipa; Ngakhale kucitira nsanje amphulupulu;
20
Pakuti woipayo sadzalandira mphotho; Nyali ya amphulupulu idzazima.
21
Mwananga, opa Yehova ndi mfumu yomwe, Osadudukira anthu osinthasintha.
22
Pakuti tsoka lao lidzaoneka modzidzimuka; Ndipo ndani adziwa cionongeko ca zaka zao?
23
Izinso ziri za anzeru. Poweruza cetera siliri labwino.
24
Wonenakwa woipa, Wolungama iwe; Magulu a anthu adzamtemberera, mitundu ya anthu idzamkwiyira,
25
Omwe amdzudzula adzasekera, Nadzadalitsika ndithu.
26
Wobwezera mau oongoka Apsompsona milomo.
27
Longosola nchito yako panjapo, nuikonzeretu kumunda; Pambuyo pace ndi kumanga nyumba yako.
28
Usacitire mnzako umboni womtsutsa opanda cifukwa; Kodi udzanyenga ndi milomo yako?
29
Usanene, Ndidzamcitira zomwezo anandicitira ine; Ndidzabwereza munthuyo monga mwa macitidwe ace.
30
Ndinapita pa munda wa wolesi, Polima mphesa munthu wosowa nzeru.
31
Taonani, ponsepo panamera minga, Ndi kuwirirapo khwisa; Chinga lace lamiyala ndi kupasuka.
32
Pamenepo ndinayang'ana ndi kuganizira, Ndinaona ndi kulandira mwambo.
33
Tulo tapang'ono, kungoodzera pang'ono, Kungomanga manja pang'ono m'kugona,
34
Ndipo umphawi wako udzafika ngati mbala; Ndi kusauka kwako ngati munthu wacikopa.
← Chapter 23
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 25 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31