bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 28
Proverbs 28
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 27
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 29 →
1
Woipaathawapalibewomthamangitsa; Koma olungama alimba mtima ngati mkango.
2
Pocimwa dziko akalonga ace acuruka; Koma anthu ozindikira ndi odziwa alikhazikikitsa nthawi yaikuru.
3
Munthu waumphawi wotsendereza osauka Akunga mvula yamadzi yokokolola dzinthu.
4
Omwe asiya cilamulo atama oipa; Koma omwe asunga cilamulo akangana nao.
5
Oipa samvetsetsa ciweruzo; Koma omwe afuna Yehova amvetsetsa zonse.
6
Waumphawi woyenda mwangwiro Apambana ndi yemwe akhotetsa njira zace, angakhale alemera.
7
Wosunga cilamulo ndiye mwana wozindikira; Koma mnzao wa adyera acititsa atate wace manyazi.
8
Wocurukitsa cuma cace, pokongoletsa ndi phindu, Angokundikira yemwe acitira osauka cisoni.
9
Wopewetsa khutu lace kuti asamve cilamulo, Ngakhale pemphero lace linyansa.
10
Wosoceretsa oongoka mtima alowe m'njira yoipa, Adzagwa mwini m'dzenje lace; Koma angwiro adzalandira colowa cabwino.
11
Wolemera adziyesa wanzeru; Koma wosauka wozindikira aululitsa zace.
12
Posekera olungama pali ulemerero wambiri; Koma pouka oipa anthu amabisala.
13
Wobisa macimo ace sadzaona mwai; Koma wakuwabvomereza, nawasiya adzacitidwa cifundo.
14
Wodala munthu wakuopakosalekeza; Koma woumitsa mtima wace adzagwa m'zoipa.
15
Monga mkango wobangula ndi cirombo coyendayenda, Momwemo mfumu yoipa ya anthu osauka.
16
Kalonga wosowa nzeru apambana kusautsa; Koma yemwe ada cisiriro adzatanimphitsa moyo wace.
17
Woparamula mlandu wakupha munthu adzathawira kudzenje; Asamuletse.
18
Woyenda mwangwiro adzapulumuka; Koma wokhota m'mayendedwe ace adzagwa posacedwa.
19
Wolima munda wace zakudya zidzamkwanira; Koma wotsata anthu opanda pace umphawi udzamkwanira.
20
Munthu wokhulupirika ali ndi madalitso ambiri; Koma wokangaza kulemera sadzapulumuka cilango,
21
Cetera siliri labwino, Ngakhale kulakwa kuti ukadye kanthu.
22
Mwini diso lankhwenzule akangaza kulemera, Osadziwa kuti umphawi udzamfikira.
23
Adzamkomera mtima wodzudzula m'tsogolo mwace, Koposa wosyasyalika ndi lilime lace.
24
Wobera atate wace, pena amace, nati, Palibe kulakwa; Ndiye mnzace wa munthu wopasula.
25
Wodukidwa mtima aputa makangano; Koma wokhulupirira Yehova adzakula.
26
Wokhulupirira mtima wace wace ali wopusa; Koma woyenda mwanzeru adzapulumuka,
27
Wogawira aumphawi sadzasowa; Koma wophimba maso ace adzatembereredwa kwambiri.
28
Pouka oipa anthu amabisala; Koma pakufa amenewo olungama acuruka.
← Chapter 27
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 29 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31