bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 9
Proverbs 9
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 8
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 10 →
1
Nzeru yamanga nyumba yace, Yasema zoimiritsa zace zisanu ndi ziwiri;
2
Yaphera nyama yace, nisanganiza vinyo wace, Nilongosolanso pa gome lace.
3
Yatuma anamwali ace, iitana Pa misanje ya m'mudzi.
4
Wacibwana yense apambukire kuno; Iti kwa yense wosowa nzeru,
5
Tiyeni, idyani cakudya canga; Nimumwe vinyo wanga ndamsanganiza.
6
Lekani, acibwana inu, nimukhale ndi moyo; Nimuyende m'njira ya nzeru.
7
Woweruza munthu wonyoza adzicititsa yekha manyazi; Yemwe adzudzula wocimwa angodetsa mbiri yace yace.
8
Usadzudzule wonyoza kuti angakude; Dzudzula wanzeru adzakukonda.
9
Ukacenjeza wanzeru adzakulitsa nzeru yace; Ukaphunzitsa wolungama adzaonjezera kuphunzira,
10
Ciyambi ca nzeru ndico kuopa Yehova; Kudziwa Woyerayo ndiko luntha;
11
Pakuti mwa ine masiku ako adzacuruka, Zaka za moyo wako zidzaonjezedwa.
12
Ukakhala wanzeru, si yako yako nzeruyo? Ndipo ukanyoza udzasauka wekha.
13
Utsiru umalongolola, Ngwa cibwana osadziwa kanthu.
14
Ukhala pa khomo la nyumba yace, Pampando pa misanje ya m'mudzi
15
Kuti uitane akupita panjira, Amene angonkabe m'kuyenda kwao,
16
Wacibwana ndani? Apambukire kuno. Ati kwa yense wopanda nzeru,
17
Madzi akuba atsekemera, Ndi cakudya cobisika cikoma.
18
Ndipo mwamunayo sadziwa kuti akufa ali konko; Omwe acezetsa utsiru ali m'manda akuya.
← Chapter 8
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 10 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31