bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
/
Proverbs 2
Proverbs 2
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
← Chapter 1
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 3 →
1
Mwananga, ukalandira mau anga, Ndi kusunga malamulo anga;
2
Kucherera makutu ako kunzeru, Kulozetsa mtima wako kukuzindikira;
3
Ukaitananso luntha, Ndi kupfuulira kuti ukazindikire;
4
Ukaifunafuna ngati siliva, Ndi kuipwaira ngati cuma cobisika;
5
Pompo udzazindikira kuopa Yehova Ndi kumdziwadi Mulungu.
6
Pakuti Yehova apatsa nzeru; Kudziwa ndi kuzindikira kuturuka m'kamwa mwace;
7
Iye asungira oongoka mtima nzeru yeniyeni; Ndiye cikopa ca oyenda molunjika;
8
Kuti acinjirize njira za ciweruzo, Nadikire khwalala la opatulidwa ace.
9
Pamenepo udzazindikira cilungamo ndi ciweruzo, Zolunjika ndi mayendedwe onse abwino.
10
Pakuti nzeru idzalowa m'mtima mwako, Moyo wako udzakondwera ndi kudziwa,
11
Kulingalira kudzakudikira, Kuzindikira kudzakucinjiriza;
12
Kukupulumutsa ku njira yoipa, Kwa anthu onena zokhota;
13
Akusiya mayendedwe olungama, Akayende m'njira za mdima;
14
Omwe asangalala pocita zoipa, Nakondwera ndi zokhota zoipa;
15
Amene apotoza njira zao, Nakhotetsa mayendedwe ao;
16
Nzeru idzakupulumutsa kwa mkazi waciwerewere, Kwa mkazi wacilendo wosyasyalika ndi mau ace;
17
Wosiya bwenzi la ubwana wace, Naiwala cipangano ca Mulungu wace;
18
Nyumba yace itsikira kuimfa, Ndi mayendedwe ace kwa akufa;
19
Onse akunka kwa iye sabweranso, Safika ku njira za moyo;
20
Nzeru idzakuyendetsa m'njira ya anthu abwino, Kuti usunge mayendedwe a olungama.
21
Pakuti oongoka mtima adzakhala m'dziko, Angwiro nadzatsalamo.
22
Koma oipa adzalikhidwa m'dziko, Aciwembu adzazulidwamo.
← Chapter 1
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 3 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31