bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Deuteronomy 34
Deuteronomy 34
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 33
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
1
Mose adakwera phiri la Nebo kuchokera ku zigwa za Mowabu. Adakafika mpaka pamwamba pa phiri la Pisiga kuvuma kwa Yeriko. Ndipo kumeneko Chauta adamuwonetsa dziko lonse, dziko la Giliyadi mpaka ku dziko la Dani.
2
Dziko lonse la Nafutali, maiko onse a Efuremu ndi Manase, ndi dziko la Yuda mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu.
3
Adamuwonetsanso chigawo chakumwera cha Negebu, ndi chigwa chimene chimafika mpaka ku Yeriko, mzinda wa mitengo ya migwalangwa, mpaka ku Zowari.
4
Tsono Chauta adauza Mose kuti, “Ilo ndilo dziko limene lija ndidalonjeza Abrahamu, Isaki ndi Yakobe, kuti ndidzapatsa zidzukulu zao. Ndakulola kuti uliwone, koma kuloŵamo kokha sindikulola.”
5
Choncho Mose, mtumiki wa Chauta, adamwalira kumeneko m'dziko la Mowabu, monga momwe Chauta adanenera.
6
Chauta adamuika ku Mowabu komweko m'chigwa, moyang'anana ndi mudzi wa Betepeori. Koma palibe ndi mmodzi yemwe amene akudziŵa malo enieni a mandawo.
7
Mose adamwalira ali wa zaka 120. Koma anali wamphamvube, ndipo maso ake anali akuthwabe.
8
Aisraele adalira maliro ake masiku makumi atatu m'chigwa cha Mowabu. Ndipo nthaŵi yolira maliro idatha.
9
Tsono Yoswa, mwana wa Nuni, adadzazidwa ndi nzeru, chifukwa Mose adaamsanjika manja kuti aloŵe m'malo mwake. Aisraele adamvera Yoswa, ndi kutsata malamulo onse amene Chauta adaŵapatsa kudzera mwa Mose.
10
Kuyambira pamenepo, sadakhaleponso mneneri wina aliyense wonga Mose. Chauta ankalankhula naye pamasompamaso.
11
Palibe mneneri wina aliyense amene adachitapo zozizwitsa ndi zodabwitsa monga zimene Chauta adauza Mose kuti achite pamaso pa mfumu ya ku Ejipito, ndi pa akulu ake, ndi m'dziko lake lonse.
12
Palibe mneneri wina aliyense amene adachita zinthu zazikulu ndi zoopsa zonga zimene adachita Mose pamaso pa Aisraele onse.
← Chapter 33
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34