bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
/
Job 3
Job 3
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
← Chapter 2
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 4 →
1
Atatero, Yobu anatsegula pakamwa pake, natemberera tsiku lake.
2
Nalankhula Yobu nati,
3
Litayike tsiku lobadwa ine, ndi usikuwo udati, Waima naye mwana wamwamuna.
4
Tsiku lija likhale mdima; Mulungu asalifunse kumwamba, ndi kuunika kusaliwalire.
5
Mdima ndi mthunzi wa imfa ziliyese laolao; mtambo ulikhalire; zonse zodetsa usana bii ziliopse.
6
Usiku uja, mdima weniweni uugwere; usakondwerere mwa masiku a m'chaka; usalowe m'chiwerengedwe cha miyezi.
7
Ha! Usiku uja ukhale chumba; kuimbira kokondwera kusalowe m'mwemo.
8
Autemberere iwo akutemberera usana, Odziwa kuutsa Leviyatani.
9
Nyenyezi za chizirezire zide; uyembekezere kuunika, koma kuusowe; usaone kephenyuka kwa mbandakucha;
10
popeza sunatseka pa makomo ake mimba ya mai wanga. Kapena kundibisira mavuto pamaso panga.
11
Ndinalekeranji kufera m'mimba? Ndi kupereka mzimu wanga pobadwa ine.
12
Anandilandiriranji maondo? Kapena mawere kuti ndiyamwe?
13
Pakuti ndikadagona pansi pomwepo ndi kukhala chete; ndikanagona tulo; pamenepo ndikadaona popumula;
14
pamodzi ndi mafumu ndi maphungu a padziko, akudzimangira m'mabwinja;
15
kapena pamodzi ndi akalonga eni ake a golide, odzaza nyumba zao ndi siliva;
16
Kapena ngati nsenye yobisika ndikadakhala kuli zii; ngati makanda osaona kuunika.
17
Apo oipa aleka kumavuta; ndi apo ofooka mphamvu akhala m'kupumula.
18
Apo a m'kaidi apumula pamodzi, osamva mau a wofulumiza wao.
19
Ang'ono ndi akulu ali komwe; ndi kapolo amasuka kwa mbuyake.
20
Amninkhiranji kuunika wovutika, ndi moyo kwa iye wakuwawa mtima,
21
wakuyembekezera imfa, koma kuli zii, ndi kuikumba koposa chuma chobisika,
22
wakusekerera ndi chimwemwe ndi kukondwera pakupeza manda?
23
Amuonetseranji kuunika munthu wa njira yobisika, amene wamtsekera Mulungu?
24
Pakuti ndikati ndidye, kumadza kuusa moyo kwanga; ndi kudzuma kwanga kumathiridwa ngati madzi.
25
Pakuti chimene ndinachiopa chandigwera, ndi chimene ndachita nacho mantha chandidzera.
26
Wosakhazikika, ndi wosakhala chete, ndi wosapumula ine, koma mavuto anandidzera.
← Chapter 2
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 4 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42