bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
/
Job 40
Job 40
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
← Chapter 39
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 41 →
1
Ndipo Yehova anabwereza kwa Yobu, nati,
2
Kodi wodzudzulayo atsutsane ndi Wamphamvuyonse? Wochita makani ndi Mulungu ayankhe.
3
Pamenepo Yobu anayankha Yehova nati,
4
Taonani, ndakhululuka ine, ndidzakubwezerani mau otani? Ndigwira pakamwa.
5
Ndalankhula kamodzi, koma sindidzayakha; inde kawiri, koma sindionjezanso.
6
Ndipo Yehova anamyankha Yobu m'kamvulumvulu, nati,
7
Dzimangire m'chuuno tsono ngati mwamuna; ndidzakufunsa, undidziwitse.
8
Chingakhale chiweruzo changa udzachithyola kodi? Udzanditsutsa kuti ndili woipa kodi, kuti ukhale wolungama ndiwe?
9
Kodi uli nalo dzanja ngati Ine Mulungu? Kapena ukhoza kugunda ndi mau ngati Ine?
10
Udzikometsere tsono ndi ukulu ndi kukuzika, nuvale ulemu ndi ulemerero.
11
Tsanulira mkwiyo wako wosefuka, nupenyerere aliyense wodzikuza ndi kumchepetsa.
12
Upenyerere aliyense wodzikuza, numtsitse, nupondereze oipa pomwe akhala.
13
Uwakwirire pamodzi m'fumbi, uzimange nkhope zao pobisika.
14
Pamenepo inenso ndidzakuvomereza, kuti dzanja lakolako lamanja likupulumutsa.
15
Tapenya tsono mvuu ndinaipanga pamodzi ndi iwe, ikudya udzu ngati ng'ombe.
16
Tapenya tsono, mphamvu yake ili m'chuuno mwake, ndi kulimbalimba kwake kuli m'mitsempha ya m'mimba yake.
17
Igwedeza mchira wake ngati mkungudza; mitsempha ya ntchafu zake ipotana.
18
Mafupa ake akunga misiwe yamkuwa; ziwalo zake zikunga zitsulo zamphumphu.
19
Iyo ndiyo chiyambi cha machitidwe a Mulungu; wakuilenga anaininkha lupanga lake.
20
Pakuti mapiri aiphukitsira chakudya, kumene zisewera nyama zonse za kuthengo.
21
Igona pansi patsinde pa mitengo yamthunzi, pobisala pabango ndi pathawale.
22
Mitengo yamthunzi iiphimba ndi mthunzi wao, misondodzi ya kumtsinje iizinga.
23
Taona madzi a mumtsinje akakula, siinjenjemera; ilimbika mtima, ngakhale Yordani atupa mpaka pakamwa pake.
24
Ikakhala maso, munthu adzaigwira kodi? Kapena kuboola m'mphuno mwake ili m'khwekhwe?
← Chapter 39
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 41 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42