bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
/
Job 41
Job 41
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
← Chapter 40
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 42 →
1
Kodi ukhoza kukoka Leviyatani ndi mbedza? Kapena kukanikiza kalandira wake ndi chingwe?
2
Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wake ndi mbedza?
3
Kodi idzachulukitsa mau akukupembedza? Kapena idzanena nawe mau ofatsa?
4
Kodi idzapangana ndi iwe, kuti uitenge ikhale kapolo wako wachikhalire?
5
Kodi udzasewera nayo ngati mbalame? Kapena udzaimangira anamwali ako kuti aiwete?
6
Kodi opangana malonda adzaitsatsa? Adzaigawana eni malonda?
7
Kodi udzadzaza khungu lake ndi ntchetho, kapena mutu wake ndi miomba?
8
Isanjike dzanja lako; ukakumbukira nkhondoyi, sudzateronso.
9
Taona, chiyembekezo chako cha pa iyo chipita pachabe. Kodi sadzatenga nkhawa munthu pakungoiona?
10
Palibe wolimba mtima kuti adzaiputa. Ndipo ndaniyo adzaima pamaso pa Ine?
11
Ndaniyo anayamba kundipatsa Ine kuti ndimthokoze? Zilizonse pansi pa thambo ponse ndi zanga.
12
Sindikhala chete osatchula ziwalo za ng'onayo, ndi mbiri ya mphamvu yake, ndi makonzedwe ake okoma.
13
Ndani adzasenda chovala chake chakunja? Adzalowa ndani kumizere iwiri ya mano ake?
14
Adzatsegula ndani zitseko za pakamwa pake? Mano ake aopsa pozungulira pao.
15
Mamba ake olimba ndiwo kudzitama kwake; amangika pamodzi ngati okomeredwatu.
16
Alumikizana lina ndi linzake, mphepo yosalowa pakati pao.
17
Amamatirana lina ndi linzake, agwirana osagawanikana.
18
Pakuyetsemula ing'anipitsa kuunika, ndi maso ake akunga zikope za m'mawa.
19
M'kamwa mwake mutuluka miuni, mbaliwali za moto zibukamo.
20
M'mphuno mwake mutuluka utsi, ngati nkhali yobwadamuka ndi moto wa zinyatsi
21
mpweya wake uyatsa makala, ndi m'kamwa mwake mutuluka lawi la moto.
22
Kukhosi kwake kukhala mphamvu, ndi mantha avumbuluka patsogolo pake.
23
Nyama yake yopsapsala igwirana ikwima pathupi pake yosagwedezeka.
24
Mtima wake ulimba ngati mwala, inde ulimba ngati mwala wa mphero.
25
Ikanyamuka, amphamvu achita mantha; chifukwa cha kuopsedwa azimidwa nzeru.
26
Munthu akaiyamba ndi lupanga, ligoma; ngakhale nthungo, kapena muvi, kapena mkondo.
27
Chitsulo ichiyesa phesi, ndi mkuwa ngati mtengo woola.
28
Muvi suithawitsa, miyala ya pachoponyera iisandutsa chiputu.
29
Zibonga ziyesedwa chiputu, iseka kuthikuza kwake kwa nthungo.
30
Kumimba kwake ikunga mapale akuthwa, itasalala kuthope ngati chopunthira.
31
Ichititsa nthubwinthubwi pozama ngati nkhali, isanduliza nyanja ikunge mafuta.
32
Ichititsa mifunde yonyezimira pambuyo pake; munthu akadati pozama pali ndi imvi.
33
Pa dziko lapansi palibe china cholingana nayo, cholengedwa chopanda mantha.
34
Ipenya chilichonse chodzikuza, ndiyo mfumu ya zodzitama zonse.
← Chapter 40
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 42 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42