bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Job 17
Job 17
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 16
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 18 →
1
Mtima wanga wasweka ndipo masiku anga atha, manda andiyasamira kukamwa.
2
Ndithudi, pali ondiseka ponseponse pondizungulira, ndikupenya m'mene akundinyozera.
3
“Inu nokha Mulungu, mukhale ngati chigwiriro changa. Kulibenso wina woti nkunditchinjiriza.
4
Inu mwatseka mitima yao kuti asamvetsetse bwino zanzeru, choncho musalole kuti iwowo apambane.
5
Paja akuti munthu akapereka abwenzi ake chifukwa cha chuma, ana ake amazunzika.
6
“Andisandutsa chisudzo chochiseka anthu, akandiwona amangoti malovu nzee.
7
M'maso mwanga mwada ndi chisoni, ndaonda ndi mutu womwe.
8
Anthu olungama akudabwa nazo kwambiri zimenezi. Anthu osachimwa akupsera mtima anthu osamvera Mulungu.
9
Komabe anthu olungama enieni amapitirira m'njira zao, anthu osalakwa amalimbikira kukhalabe oyera.
10
“Tsono nonsenu bwerani, mubwereze mau anu, pakati panupa sindidzapezapo ndi mmodzi yemwe wanzeru.
11
Masiku anga atha, ndipo zimene ndidaakonza zalephereka. Zimene ndinkayembekeza zapita padera.
12
Koma abwenzi anga amanena kuti usiku ndi usana womwe. Amati, ‘kuŵala ndiye kuli pafupi,’ chonsecho mdima uli goo.
13
Chimene ndikuyembekeza ndicho kukakhala ku manda, ndikayaleko mphasa yanga mumdima.
14
Ndidzauza dzenje la manda kuti, ‘Iwe ndiwe bambo wanga.’ Ndidzalankhulanso ndi mphutsi kuti, ‘Ndiwe mai wanga,’ kapena kuti, ‘Ndiwe mlongo wanga.’
15
Tsono chiyembekezo changa chili kuti? Ndani angaone populumukira panga?
16
Ndithu, sindidzakhalanso ndi chiyembekezo chilichonse poloŵa m'manda, pamene ndidzatsikira ku fumbi.” Bilidadi
← Chapter 16
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 18 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42