bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Job 18
Job 18
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 17
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 19 →
1
Tsono Bilidadi wa ku Suki adayankha kuti,
2
“Kodi iwe Yobe, ukhala mpaka liti ukufunafuna zonena? Ingokhala chete, umvetsere, ndipo ife tilankhula.
3
Chifukwa chiyani ukutiyesa opusa ngati ng'ombe? Chifukwa chiyani tikuwoneka ngati opanda nzeru m'maso mwako?
4
Iwe ukungodzipweteka ndi mkwiyo wako. Kodi dziko lapansi lidzasanduka bwinja chifukwa choti iweyo uli wokwiya? Kodi thanthwe nkudzachotsedwa pamalo pake, kuti likukondweretse iweyo?
5
“Nyale ya munthu woipa yazima, malaŵi a moto wake sakuŵalanso.
6
Kuŵala kwa m'nyumba mwake kwasanduka mdima, ndipo nyale ya pambali pake yazima.
7
Kale ankayenda ndi mgugu, koma tsopano wakhumudwa. Nzeru zake zomwe zamgwetsa.
8
Mapazi ake omwe amloŵetsa mu ukonde, ndipo wakodwa. Tsono kuti achokemo, wagweranso m'mbuna.
9
Msampha wamkola mwendo, ndipo khwekhwe lamgwira.
10
Amtchera msampha pansi mobisika, amtchera diŵa m'njira.
11
Zoopsa zikumchititsa mantha pa mbali zonse, zikumtsatira pambuyo pake.
12
Adaali ndi mphamvu, koma tsopano ali ndi njala. Tsoka likumdikira nthaŵi zonse.
13
Wagwidwa nthenda yoopsa thupi lonse, miyendo yake, manja ake, zonse zaola.
14
Amuchotsa m'nyumba mwake m'mene ankadalira. Amkokera kwa Imfa, mfumu ya zoopsa zonse.
15
M'nyumba mwake zake zonse zachotsedwamo, awazamo sulufule, kuti aphe tizilombo ta matenda.
16
Mizu yake ikuuma pansi, nthambi zake zikufota.
17
Sadzamkumbukiranso kwao kapena kwina kulikonse, dzina lake lidzaiŵalika.
18
Adzamchotsa m'dziko la amoyo ndi kumponya mu mdima, adzampirikitsa pa dziko lapansi.
19
Sadzaona zidzukulu m'banja mwake. Sikudzaoneka ana otsala kumene ankakhalako.
20
Anthu akuzambwe adabwa nalo tsoka lakelo, anthu akuvuma nawonso akungopukusa mitu.
21
Ndithu zimenezi ndizo zimagwera anthu oipa. Kumeneku ndiye kutha kwake kwa anthu osasamala za Mulungu.” Yobe
← Chapter 17
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 19 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42