bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Job 35
Job 35
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 34
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 36 →
1
Elihu adaonjeza kuti,
2
“Kodi mukuganiza kuti mukukhoza: Kunena kuti, ‘Ndine wolungama pamaso pa Mulungu?’
3
Kapena kufunsa kuti, ‘Kodi kuchimwa kwanga ubwino wake ndi wotani? Nanga ndikadapindulanji ndikadaleka kuchimwa?’
4
Ndidzakuyankhani inuyo ndi abwenzi anu omwe.
5
Muyang'ane kumwamba, ndipo muwone mitambo imene ili kutali ndi inuyi.
6
Kodi mukamachimwa, ndiye kuti mukumchita Mulungu chiyani? Mukamachulukitsa machimo anu, kodi mumamvuta bwanji?
7
Kodi mukati ndinu wosalakwa, ndiye kuti mukumpindulira chiyani? Kodi angathe kulandiranji kwa inu?
8
Kuipa kwanu kumangovuta anthu anzanu, chimodzimodzinso ntchito zanu zabwino zimangopindulira anzanu basi.
9
“Anthu akufuula chifukwa cha kuzunzidwa. Akupempha chithandizo chifukwa anthu amphamvu akuŵavula.
10
Koma palibe wonena kuti, ‘Kodi ali kuti Mulungu, Mlengi wanga, amene amatithandiza ngakhale pakati pa mdima wa mavuto,
11
amenenso amatiphunzitsa kupambana nyama zam'dziko ndipo amatipatsa nzeru kupambana mbalame zouluka.’
12
Ena amaitana Mulungu koma Iye saŵayankha, chifukwa cha kunyada ndi kuipa kwa anthuwo.
13
Ndithudi, Mulungu saamva kupempha kopanda pake, Mphambe sasamalako zimenezo.
14
“Inu aYobe, mukunena kuti simungathe kupenya Mulungu, komabe mlandu wanu adzauzenga ndiye, ndipo mukudikira kuti augamule.
15
Ndiye tsono, popeza kuti ukali wake sukupereka chilango, ndipo akuchita ngati sasamalako kwambiri zochita zoipa za anthu,
16
inu aYobe mumangolankhula zopandapake, mukungochulukitsa mau opanda nzeru.”
← Chapter 34
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 36 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42