bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Job 23
Job 23
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 22
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 24 →
1
Apo Yobe adayankha kuti,
2
“Leronso ndikudandaula kwambiri kwa Mulungu. Ngakhale ndikubuula, Mulungu akundilangiralangira ndithu.
3
Ha, ndikadadziŵa kumene ndikadampeza Mulungu, kuti ndikafike mpaka komwe amakhalako!
4
Ndikadakamba mlandu wanga pamaso pake, bwenzi nditafotokoza zifukwa zanga zonse.
5
Bwenzi nditamva mau amene akadandiyankha, bwenzi nditamvetsa zimene akadandiwuza.
6
Kodi Mulungu akadalimbana nane ndi mphamvu zake? Ai, koma akadamva mau anga.
7
Kumeneko munthu wolungama akadalankhula ndi Iye modekha. Wondiweruzayo akadandipeza wosalakwa nthaŵi zonse.
8
“Taonani, ndikapita chakutsogolo, Iye kulibe kumeneko, ndikabwerera cham'mbuyo, sinditha kumupenya.
9
Ndimamfunafuna kumanzere, koma osamuwona. Ndimayang'ananso kumanja, koma osampenya ndithu.
10
Komabe Mulungu amadziŵa m'mene ndimayendera, akandiyesa adzapeza kuti ndine wangwiro ngati golide.
11
Mapazi anga akuponda m'mapazi mwake, ndasunga njira yake, ndipo sindidaitaye.
12
Sindidapatuke kusiya malamulo ake. Ndasunga mau a pakamwa pake kupambana zofuna zanga zonse.
13
“Iyeyo ndi wosasinthika, nanga ndani angathe kumsintha maganizo? Zimene wafuna, amazichitadi.
14
Zimene adatsimikiza kuti adzandichita, adzachitadi, ndipo amalingalira zambiri zoterezi.
15
Nchifukwa chake ndikuchita mantha kwambiri pamaso pake. Ndikaganiza za iyeyo, ndimaopa kwabasi.
16
Mulungu walefula mtima wanga. Mphambe wandiwopsa.
17
Wandichititsa mantha ndi Mulungu, osati mdima wa mavuto onse amene amandiphimbaŵa.”
← Chapter 22
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 24 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42