bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Job 8
Job 8
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 7
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 9 →
1
Apo Bilidadi, Msuhi, adayankha Yobe kuti,
2
“Kodi udzakhala ukulankhulabe zoterezi mpaka liti? Mau akoŵa akungopita ngati mphepo.
3
Kodi Mulungu amapotoza kuweruza kwake? Kodi Mphambe amalephera kuchita zachilungamo?
4
Kapena ana ako adamchimwira, nkuwona Mulungu adaŵalanga chifukwa cha zochimwa zaozo.
5
Ngati iwe uchita zimene Mulungu afuna, ngati upemba kwa Mphambe,
6
ngati ukhala wangwiro ndi wolungama, ndithudi Mulungu adzachitapo kanthu, nkukuthandiza. Adzakubwezera zabwino zonse ngati mphotho yokuyenerera.
7
Chiyambi chako chidzaoneka ngati chochepa, kuyerekeza ndi m'mene udzakhalira komaliza.
8
“Tsono ndikukupempha kuti ufunsefunse kwa anthu amvulazakale, usinkhesinkhe zimene makolo athu adakumana nazo.
9
Ife ndife adzulodzuloli, sitidziŵa kanthu ai. Moyo wathu pa dziko lapansi uli ngati chithunzithunzi.
10
Kodi anthu amvulazakalewo nkupanda kukuphunzitsa? Kodi iwo nkupanda kukuuza zinthu? Pajatu mau a akulu akoma akagonera.
11
“Kodi gumbwa nkumera pa nthaka yopanda chinyontho? Nanga bango nkukondwa kumene kulibe madzi?
12
Popanda madzi zimenezi zimafota zikali zaziŵisi ndi zosadula, zimauma msanga kupambana chomera china chilichonse.
13
Ndimo m'mene zimaŵachitikira anthu oiŵala Mulungu. Chikhulupiriro cha munthu wosapembedza Mulungu chimatha.
14
Kulimba mtima kwake kumafooka, zimene amakhulupirira zili ngati ukonde wa kangaude.
15
Amatsamira pa nyumba yake, koma nyumbayo si yolimba konse. Amaigwiritsa, komabe siikhalitsa.
16
Munthu woipayo ali ngati zomera zokondwa ngakhale mpadzuŵa pomwe, ndipo nthambi zake zimatambalala pa munda wake.
17
Mizu yake imayanga pa miyala, ndipo imakangamira pa thanthwe.
18
Koma mutamchotsa pamalo pakepo, palibe ndi mmodzi yemwe angadziŵe kuti iyeyo anali pamenepo.
19
Zokondwetsa zokhazo ndizo zidzakhala phindu la ntchito zake, kenaka ena adzabwera kudzaloŵa m'malo mwake.
20
“Ndithu Mulungu sangamkane munthu wopanda cholakwa, komanso anthu olakwa Mulungu sangaŵathandize konse.
21
Iye adzadzaza chiphwete m'kamwa mwako, ndipo udzafuula mokondwa.
22
Amene amadana nawe adzachita manyazi, malo okhalako anthu oipa sadzaonekanso.” Yobe
← Chapter 7
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 9 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42