bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Job 32
Job 32
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 31
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 33 →
1
Tsono anthu atatu aja adaleka osamulankhuzanso Yobe, chifukwa choti iyeyo adaadziwona kuti ndi wosachimwa.
2
Koma Elihu, mwana wa Barakele, wa fuko la Buzi, wa banja la Ramu, adapsera mtima Yobe chifukwa chodziyesa wolungama kupambana Mulungu.
3
Adapseranso mtima abwenzi ake atatu aja, chifukwa choti sadathe kuyankha, ngakhale iwo omwe adaapeza kuti Yobeyo ndi wolakwa.
4
Koma Elihu adadikira kuti alankhule ndi Yobe, chifukwa choti abwenziwo anali akuluakulu kupambana iyeyo.
5
Tsono ataona kuti anthu atatuwo sadamuyankhe Yobe moyenera, adapsa mtima.
6
Choncho Elihu, mwana wa Barakele wa fuko la Buzi, adayamba kulankhula, adati, “Ine ndine wamng'ono, inuyo ndinu akuluakulu. Nkuwona ndinkaopa, ndipo ndinkachita mantha kuti ndikuuzeni zakukhosi.
7
Ndinkati ayambe ndi akuluakulu aja kulankhula, chifukwa amvulazakale ndiwo amaphunzitsa nzeru.
8
Koma mzimu wa Mphambe ndiwo umaloŵa mwa anthu ndi kuŵapatsa nzeru.
9
Sikuti ukalamba wokha ndiwo umasandutsa anthu kuti akhale anzeru, si kukhwima kokha kumene kumachititsa kuti anthu azimvetsa zimene zili zoyenera.
10
Nchifukwa chaketu ndikuti, ‘Mundimve, lekeni ndinenepo maganizo anga.’
11
“Zoona, ndinkadikira mau anuwo, ndinkafuna kumvetsera mau ogwira mtima pamene inuyo munkafunafuna zanzeru zoti mulankhule.
12
Ndidakumvetseranidi, koma panalibe ndi mmodzi yemwe mwa inu amene adatsutsa mau a Yobe, panalibe amene adayankhako nkomwe.
13
Chenjerani, musanene kuti, ‘Ife tapeza nzeru, Mulungu ndiye angamgonjetse, osati munthu ai.’
14
Yobe sadalankhule ndi ine, ndipo ine sindimuyankha monga m'mene mwamuyankhira inu.”
15
“Iwowo asokonezeka, sakuyankhanso. Alibe ndi mau omwe oti angalankhule.
16
Kodi ine ndidikire chifukwa iwo sakulankhula, kodi ndisayankhekonso poti iwo angoti phee?
17
Ai, ine ndiyankhapo tsopano. Nanenso ndilankhula zakukhosi.
18
Pakuti ndili nawo mau ambiri, mtima wanga ukundichichiza kuti ndilankhule.
19
Ndithudi, maganizo adzaza mumtima mwanga ali ngati vinyo wopanda pompungulira, ineyo ndili ngati matumba atsopano achikopa ofuna kuphulika ndi vinyo.
20
Ndiyenera kulankhula kuti mtima utsike. Pakufunika kuti ndiyankhepo pa nkhaniyi.
21
Sindiwonetsa kukondera munthu wina aliyense, sindilankhula zoshashalika.
22
Ine sindidziŵa kulankhula mochenjera, kuwopa kuti Mlengi wanga angandilange msanga.” Elihu adzudzula Yobe kuti ndi wodzikuza.
← Chapter 31
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 33 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42