bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Jeremiah 39
Jeremiah 39
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 38
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 43
Chapter 44
Chapter 45
Chapter 46
Chapter 47
Chapter 48
Chapter 49
Chapter 50
Chapter 51
Chapter 52
Chapter 40 →
1
Pa chaka chachisanu ndi chinai cha ufumu wa Zedekiya ku Yuda, mwezi wakhumi, Nebukadinezara, mfumu ya ku Babiloni, adadza ndi gulu lake lonse lankhondo ku Yerusalemu, nazinga mzindawo.
2
Pa chaka chakhumi ndi chimodzi cha ufumu wa Zedekiya, mwezi wachinai, tsiku lachisanu ndi chinai la mweziwo, malinga a mzindawo adabooledwa.
3
Pamenepo akuluakulu onse a mfumu ya ku Babiloni adaloŵa nakakhala pa chipata chapakati. Anali aŵa: Neregali-Sarezere, Samugiri-Nebo, Sarisekimu mkulu wa nduna, ndi Neregali-Sarezere winanso mkulu wolamulira gulu lankhondo lapatsogolo, pamodzi ndi akuluakulu ena onse a mfumu ya ku Babiloni.
4
Pamene Zedekiya, mfumu ya ku Yuda, adaŵaona, iyeyo pamodzi ndi ankhondo ake adathaŵa mumzindamo usiku, kudzera ku munda wa mfumu, kubzola pa chipata cha pakati pa zipupa ziŵiri. Adathaŵira ku Araba.
5
Koma gulu lankhondo la Ababiloni lidamlondola ndi kukamgwira Zedekiyayo ku zigwa za ku Yeriko. Mfumuyo ataigwira, adapita nayo kwa Nebukadinezara, mfumu ya ku Babiloni, ku Ribula m'dziko la Hamati. Ndipo adagamula mlandu wake komweko.
6
Tsono mfumu ya ku Babiloni idapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribula, iyeyo akuwona. Idaphanso atsogoleri onse a ku Yuda.
7
Kenaka idamkolowola maso Zedekiyayo, nimmanga ndi maunyolo nkupita naye ku Babiloni.
8
Ababiloni adatentha nyumba yaufumu, Nyumba ya Chauta pamodzi ndi nyumba zina zonse za anthu. Ndipo adagwetsa malinga a Yerusalemu.
9
Nebuzaradani, mtsogoleri wa alonda ankhondo, adatenga anthu onse otsala a mumzindawo kupita nawo ku Babiloni. Ameneŵa ndiwo amene adaadzipereka kwa iye, ndiponso anthu amene adaatsalira.
10
Nebuzaradani, mtsogoleri wa alonda ankhondoyo, adasiya anthu okhaokha osauka kwambiri, ndi opanda nkanthu komwe m'dziko la Yuda. Ndipo adaŵapatsa minda yamphesa ndi minda inanso.
11
Nebukadinezara, mfumu ya ku Babiloni, adatumiza mau kwa Nebuzaradani mtsogoleri wa alonda ankhondo, onena za Yeremiya. Adati,
12
“Mtenge, umsamale bwino, usamvute, koma umchitire zimene afuna.”
13
Motero Nebuzaradani, mtsogoleri wa alonda ankhondo uja, adanyamuka pamodzi ndi Nebusazibani mtsogoleri wamkulu, Neregali-Sarezere mkulu wolamulira gulu lankhondo linanso ndi akuluakulu onse a mfumu ya ku Babiloni.
14
Iwowo adakatenga Yeremiya ku bwalo la alonda, nakampereka kwa Gedaliya, mwana wa Ahikamu, mdzukulu wa Safani, kuti amumasule ndi kumtumiza kunyumba kwake. Motero Yeremiya adakakhala ndi anthu ake.
15
Chauta adalankhula ndi Yeremiya pamene anali m'ndende ku bwalo la alonda. Adati,
16
“Pita ukauze Ebedemeleki Mkusi uja kuti Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele akunena kuti, ‘Zidzachitikadi zimene ndidaanena za mzinda uno, ndipo nzoipa osati zabwino, ai. Zidzachitikadi pa nthaŵi yake, iwe ukupenya.
17
Iweyo ndidzakupulumutsa tsiku limenelo, ndipo sudzaperekedwa kwa anthu amene umaŵaopa.
18
Ndithu ndidzakupulumutsa, ndipo sudzaphedwa pa nkhondo. Udzapulumuka chifukwa choti wandikhulupirira,’ ” akuterotu Chauta.
← Chapter 38
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 43
Chapter 44
Chapter 45
Chapter 46
Chapter 47
Chapter 48
Chapter 49
Chapter 50
Chapter 51
Chapter 52
Chapter 40 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42
43
44
45
46
47
48
49
50
51
52