bible
ra
🌐 Language
English
Español
Français
Deutsch
Português
Italiano
Nederlands
Русский
中文
日本語
한국어
العربية
Türkçe
Tiếng Việt
ไทย
Indonesia
All Languages
Home
/
Chewa
/
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
/
Genesis 5
Genesis 5
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
← Chapter 4
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 43
Chapter 44
Chapter 45
Chapter 46
Chapter 47
Chapter 48
Chapter 49
Chapter 50
Chapter 6 →
1
Mndandanda wa mibadwo yochokera mwa Adamu udayenda motere: (Mulungu polenga Adamu, adampanga muchifaniziro chake.
2
Adalenga mwamuna ndi mkazi, ndipo adaŵadalitsa, naŵatchula dzina loti Anthu.)
3
Adamu ali wa zaka 130 adabereka mwana wofanafana ndi iye, namutcha Seti.
4
Pambuyo pake Adamu adakhala ndi moyo zaka zinanso 800. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
5
Adamwalira ali wa zaka 930.
6
Seti ali wa zaka 105, adabereka mwana dzina lake Enosi,
7
ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 807. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
8
Adamwalira ali wa zaka 912.
9
Enosi ali wa zaka 90, adabereka mwana dzina lake Kenani,
10
ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 815. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
11
Adamwalira ali wa zaka 905.
12
Kenani ali wa zaka 70, adabereka mwana dzina lake Mahalalele,
13
ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 840. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
14
Adamwalira ali wa zaka 910.
15
Mahalalele ali wa zaka 65 adabereka Yaredi,
16
ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 830. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
17
Adamwalira ali wa zaka 895.
18
Yaredi ali wa zaka 162, adabereka mwana dzina lake Enoki,
19
ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 800. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
20
Adamwalira ali wa zaka 962.
21
Enoki ali wa zaka 65, adabereka mwana dzina lake Metusela.
22
Enoki adakhala ndi moyo zaka zina 300, akuyanjana ndi Mulungu. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
23
Adamwalira ali wa zaka 365.
24
Iyeyu adayanjana ndi Mulungu moyo wake wonse. Ndipo sadaonekenso, chifukwa choti Mulungu adamtenga.
25
Metusela ali wa zaka 187, adabereka mwana dzina lake Lameki,
26
ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 782. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
27
Adamwalira ali wa zaka 969.
28
Lameki ali wa zaka 182, adabereka mwana,
29
ndipo adati, “Mwana ameneyu adzatipumuza ku ntchito zathu zolemetsazi zolima nthaka imene Chauta adaitemberera.” Ndipo mwanayo adamutcha dzina lake Nowa.
30
Lameki adakhalanso ndi moyo zaka zina 595. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
31
Adamwalira ali wa zaka 777.
32
Nowa ali wa zaka zopitirira 500, adabereka ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti.
← Chapter 4
Jump to:
Chapter 1
Chapter 2
Chapter 3
Chapter 4
Chapter 5
Chapter 6
Chapter 7
Chapter 8
Chapter 9
Chapter 10
Chapter 11
Chapter 12
Chapter 13
Chapter 14
Chapter 15
Chapter 16
Chapter 17
Chapter 18
Chapter 19
Chapter 20
Chapter 21
Chapter 22
Chapter 23
Chapter 24
Chapter 25
Chapter 26
Chapter 27
Chapter 28
Chapter 29
Chapter 30
Chapter 31
Chapter 32
Chapter 33
Chapter 34
Chapter 35
Chapter 36
Chapter 37
Chapter 38
Chapter 39
Chapter 40
Chapter 41
Chapter 42
Chapter 43
Chapter 44
Chapter 45
Chapter 46
Chapter 47
Chapter 48
Chapter 49
Chapter 50
Chapter 6 →
All chapters:
1
2
3
4
5
6
7
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42
43
44
45
46
47
48
49
50